Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp20 No. 3 tsamba 3
  • Mungasangalale ndi Madalitso Osatha Ochokera kwa Mulungu Wachikondi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mungasangalale ndi Madalitso Osatha Ochokera kwa Mulungu Wachikondi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Mukamawerenga nkhani zotsatirazi tikukupemphani kuti muganizire mafunso awa:
  • Mawu Oyamba
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Ngozi Zadzidzidzi?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Madalitso Akuru Ali Pafupi Kwenikweni!
    Coonadi Cimene Cimatsogolera ku Moyo Wamuyaya
  • Mukhoza Kusangalala ndi Madalitso Ochokera kwa Mlengi Wathu Mpaka Kalekale
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
wp20 No. 3 tsamba 3
Banja likucheza mosangalala. Makolo akhala pampando atagwirana manja ndipo ana akujambula zithunzi.

Mungasangalale ndi Madalitso Osatha Ochokera kwa Mulungu Wachikondi

  • Kodi mumalakalaka mutakhala m’dziko lopanda nkhondo, chiwawa ndi chidani?

  • Kodi mumafunitsitsa mutaona matenda, kuvutika ndi imfa zitatheratu?

  • Kodi mumalakalaka mutakhala moyo popanda kudandaula ndiponso kuda nkhawa?

  • Kodi mumafuna mutakhala pamalo amene sangawonongedwe ndi ngozi za m’chilengedwe?

Mulungu wathu wachikondi yemwenso ndi Mlengi wa dziko lathu lokongolali, walonjeza kuti adzadalitsa mtundu wa anthu powapatsa moyo wamtendere komanso wachimwemwe kwamuyaya. Amenewa si maloto.

Mukamawerenga nkhani zotsatirazi tikukupemphani kuti muganizire mafunso awa:

  • Kodi Mlengi wathu amatikonda?

  • Kodi Mulungu akutiuza uthenga wotani?

  • Kodi aneneri a Mulungu ananena zotani zokhudza madalitso amene Mulungu analonjeza?

  • Kodi tingatani kuti tizikhala osangalala panopa ndiponso kuti tidzasangalale ndi madalitso osatha m’tsogolo?

Tiyeni tiyambe ndi kuona zimene Mlengi wathu amatichitira posonyeza kuti amakonda anthu

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena