SEPTEMBER 8-14
MIYAMBO 30
Nyimbo Na. 136 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Musandipatse Umphawi Kapena Chuma”
(10 min.)
Munthu amakhaladi wosangalala chifukwa chodalira Yehova, osati chifukwa choti ali ndi chuma (Miy 30:8, 9; w18.01 24-25 ¶10-12)
Munthu wadyera sakhutira (Miy 30:15, 16; w87 5/15 30 ¶8)
Mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kupewa ngongole zosafunika komanso nkhawa (Miy 30:24, 25; w11 6/1 10 ¶4)
ZIMENE MUNGACHITE PA KULAMBIRA KWA PABANJA: Monga banja, kambiranani mmene mumaonera ndalama.—w24.06 13 ¶18.
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Miy 30:26—Kodi tikuphunzira chiyani kwa mbira? (w09 4/15 17 ¶11-13)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Miy 30:1-14 (th phunziro 2)
4. Ulendo Woyamba
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Gwiritsani ntchito Nsanja ya Olonda Na. 1 2025 kuti muyambe kukambirana ndi munthu. (lmd phunziro 1 mfundo 3)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. (lmd phunziro 9 mfundo 3)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira
(4 min.) Nkhani. ijwbq nkhani na. 102—Mutu: Kodi Kutchova Juga Ndi Tchimo? (th phunziro 7)
Nyimbo Na. 80
7. Tisamapusitsidwe ndi Mtendere Wosakhalitsa—Chibisa Selemani
(5 min.) Nkhani yokambirana.
Onerani VIDIYOYI. Kenako funsani funso ili:
Kodi tikuphunzira chiyani kwa M’bale Selemani pa nkhani yosankha zinthu zomwe zingatithandize kukhala osangalala komanso okhutira?
8. Vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September
(10 min.) Onerani VIDIYOYI.
9. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) lfb mutu 16-17