1
Mawuyo anakhala munthu (1-18)
Umboni umene Yohane M’batizi anapeleka (19-28)
Yesu, Mwanawankhosa wa Mulungu (29-34)
Ophunzila oyamba a Yesu (35-42)
Filipo ndi Nataniyeli (43-51)
2
Phwando la ukwati ku Kana; asandutsa madzi kukhala vinyo (1-12)
Yesu ayeletsa kacisi (13-22)
Yesu amadziwa za mumtima mwa anthu (23-25)
3
4
Yesu ndi mayi wacisamariya (1-38)
Asamariya ambili akhulupilila Yesu (39-42)
Yesu acilitsa mwana wamwamuna wa munthu wina wotumikila mfumu (43-54)
5
Munthu wodwala acilitsidwa ku Betesida (1-18)
Yesu apatsidwa mphamvu ndi Atate wake (19-24)
Akufa adzamva mawu a Yesu (25-30)
Maumboni okamba za Yesu (31-47)
6
Yesu adyetsa anthu 5,000 (1-15)
Yesu ayenda pamadzi (16-21)
Yesu ndi “cakudya copatsa moyo” (22-59)
Ambili apunthwa ndi mawu a Yesu (60-71)
7
Yesu ku Cikondwelelo ca Misasa ca Ayuda (1-13)
Yesu aphunzitsa ku cikondwelelo (14-24)
Anthu akhala ndi maganizo osiyanasiyana pa nkhani yokhudza Khristu (25-52)
8
9
Yesu acilitsa munthu amene anabadwa wakhungu (1-12)
Munthu wocilitsidwa afunsidwa mafunso ndi Afarisi (13-34)
Khungu la Afarisi (35-41)
10
M’busa ndi makola a nkhosa (1-21)
Ayuda akumana ndi Yesu ku Cikondwelelo ca Kupatulila Kacisi (22-39)
Ayuda ambili akana kukhulupilila (24-26)
“Nkhosa zanga, zimamvela mawu anga” (27)
Mwana ndi wogwilizana ndi Atate (30, 38)
Ambili akhulupilila ku tsidya lina la Yorodano (40-42)
11
Imfa ya Lazaro (1-16)
Yesu atonthoza Marita ndi Mariya (17-37)
Yesu aukitsa Lazaro (38-44)
Akonza ciwembu cakuti aphe Yesu (45-57)
12
Mariya athila mafuta pa mapazi a Yesu (1-11)
Yesu atamandidwa polowa mu Yerusalemu (12-19)
Yesu akambilatu za imfa yake (20-37)
Kusowa cikhulupililo kwa Ayuda kukwanilitsa ulosi (38-43)
Yesu anabwela kudzapulumutsa dziko (44-50)
13
Yesu asambika mapazi a ophunzila ake (1-20)
Yesu azindikila kuti Yudasi ndiye adzamupeleka (21-30)
Lamulo latsopano (31-35)
Yesu akambilatu kuti Petulo adzamukana (36-38)
14
15
Fanizo la mtengo wa mpesa weniweni (1-10)
Lamulo la kuonetsa cikondi ngati ca Khristu (11-17)
Dziko lidana ndi ophunzila a Yesu (18-27)
16
Ophunzila a Yesu akhoza kuphedwa (1-4a)
Nchito ya mzimu woyela (4b-16)
Cisoni ca ophunzila cidzasanduka cimwemwe (17-24)
Yesu agonjetsa dziko (25-33)
17
18
Yudasi apeleka Yesu (1-9)
Petulo agwilitsa nchito lupanga (10, 11)
Yesu apelekedwa kwa Anasi (12-14)
Petulo akana Yesu koyamba (15-18)
Yesu aonekela pamaso pa Anasi (19-24)
Petulo akana Yesu kaciwili komanso kacitatu (25-27)
Yesu aonekela pamaso pa Pilato (28-40)
19
Yesu akwapulidwa ndi kunyodoledwa (1-7)
Pilato afunsanso Yesu mafunso (8-16a)
Yesu akhomeleledwa pamtengo ku Gologota (16b-24)
Yesu akonza zakuti amayi ake asamalidwe (25-27)
Imfa ya Yesu (28-37)
Yesu aikidwa m’manda (38-42)
20
Manda opanda kanthu (1-10)
Yesu aonekela kwa Mariya Mmagadala (11-18)
Yesu aonekela kwa ophunzila ake (19-23)
Thomasi akayikila koma pambuyo pake akhulupilila (24-29)
Colinga ca mpukutu uwu (30, 31)
21
Yesu aonekela kwa ophunzila ake (1-14)
Petulo atsimikizila Yesu kuti amamukonda (15-19)
Tsogolo la ophunzila okondedwa a Yesu (20-23)
Mapeto ake (24, 25)