February 19-25
MATEYU 16-17
Nyimbo 45 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kodi Muli na Maganizo a Ndani?”: (10 min.)
Mat. 16:21, 22—Cifukwa cokhudzika mtima, Petulo sanaganize bwino (w07 2/15 peji 16 pala. 17)
Mat. 16:23—Petulo sanakhale na maganizo a Mulungu (w15 5/15 peji 13 mapa. 16-17)
Mat. 16:24—Akhristu ayenela kulola maganizo a Mulungu kuwatsogolela mu umoyo wawo (w06 4/1 peji 23 pala. 9)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mat. 16:18—N’ndani anali thanthwe limene Yesu anamangapo mpingo wacikhristu? (“Iwe ndiwe Petulo, ndipo pathanthwe ili,” “mpingo” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 16:18)
Mat. 16:19—Kodi “makiyi a Ufumu wakumwamba” amene Yesu anapatsa Petulo n’ciani? (“makiyi a Ufumu wakumwamba” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 16:19)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 16:1-20
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano a citsanzo. Ndiyeno, yankhani pa zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kulalikidwa.
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelelapo) Seŵenzetsani makambilano a citsanzo.
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyo.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuseŵenzetsa Mafunso Mwaluso”: (15 min.) Kukambilana. Tambani vidiyo yakuti Gwilani Nchito Imene Yesu Anagwila—Phunzitsani.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 9
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 134 na Pemphelo