December Yophunzila Zamkatimu NKHANI YOPHUNZILA 48 Buku la Yobu Lingakuthandizeni Mukakumana ndi Mabvuto NKHANI YOPHUNZILA 49 Buku la Yobu Lingakuthandizeni Mukamapeleka Uphungu NKHANI YOPHUNZILA 50 Tengelani kudzicepetsa kwa Yehova NKHANI YOPHUNZILA 51 Mungatani Kuti Tsiku la Ukwati Wanu Likalemekeze Yehova? Inu Okalamba, Ndinu Ofunika Kwambili Mumpingo Kodi Mukukumbukila? ZIMENE MUNGACITE PA KUWELENGA KWANU Limbitsani Cikhulupililo Canu Cakuti Yehova Ali ndi Mphamvu Zokupulumutsani