Numeri 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Uwauze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, mudzandifunse ngati sindidzachita kwa inu monga mwa zimene mwakhala mukulankhula, zimene ndadzimvera ndekha m’makutu mwangamu.+ Deuteronomo 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Nthawi yonseyi Yehova anali kumvetsera mawu anu. Motero anakwiya kwambiri, ndipo analumbira+ kuti, Salimo 95:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunena za anthu amenewa ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti:+“Sadzalowa mu mpumulo wanga.”+ Ezekieli 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu+ kuti sindidzawalowetsa m’dziko limene ndinawapatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ (dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse)+ Aheberi 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nanga kodi analumbirira+ ndani kuti sadzalowa mu mpumulo wake? Kodi si omwe aja amene anachita zosamvera?+
28 Uwauze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, mudzandifunse ngati sindidzachita kwa inu monga mwa zimene mwakhala mukulankhula, zimene ndadzimvera ndekha m’makutu mwangamu.+
34 “Nthawi yonseyi Yehova anali kumvetsera mawu anu. Motero anakwiya kwambiri, ndipo analumbira+ kuti,
15 Ine ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu+ kuti sindidzawalowetsa m’dziko limene ndinawapatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ (dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse)+
18 Nanga kodi analumbirira+ ndani kuti sadzalowa mu mpumulo wake? Kodi si omwe aja amene anachita zosamvera?+