Deuteronomo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ ndipo tsopano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakuthambo.+ Salimo 105:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamene ananena zimenezi, n’kuti iwo ali ochepa.+N’kuti ali ochepa kwambiri komanso ali alendo m’dzikolo.+ Yesaya 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yang’anani kwa tate+ wanu Abulahamu,+ ndi kwa Sara+ amene anakuberekani ndi zowawa za pobereka. Abulahamuyo anali munthu mmodzi pamene ndinamuitana,+ koma ndinamudalitsa ndi kumusandutsa anthu ambiri.+
22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ ndipo tsopano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakuthambo.+
12 Pamene ananena zimenezi, n’kuti iwo ali ochepa.+N’kuti ali ochepa kwambiri komanso ali alendo m’dzikolo.+
2 Yang’anani kwa tate+ wanu Abulahamu,+ ndi kwa Sara+ amene anakuberekani ndi zowawa za pobereka. Abulahamuyo anali munthu mmodzi pamene ndinamuitana,+ koma ndinamudalitsa ndi kumusandutsa anthu ambiri.+