Oweruza 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitatero, ana a Benjamini anatuluka m’Gibeya+ ndi kupha amuna a Isiraeli 22,000 tsiku limenelo, n’kusiya mitembo yawo itagonagona pansi.+ Oweruza 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo ana a Benjamini anatuluka m’Gibeya kudzakumana nawo tsiku lachiwirilo, ndipo anaphanso amuna ena 18,000 mwa ana a Isiraeli, n’kusiya mitembo yawo itagonagona pansi.+ Ophedwa onsewa anali amuna ogwira lupanga.+
21 Zitatero, ana a Benjamini anatuluka m’Gibeya+ ndi kupha amuna a Isiraeli 22,000 tsiku limenelo, n’kusiya mitembo yawo itagonagona pansi.+
25 Pamenepo ana a Benjamini anatuluka m’Gibeya kudzakumana nawo tsiku lachiwirilo, ndipo anaphanso amuna ena 18,000 mwa ana a Isiraeli, n’kusiya mitembo yawo itagonagona pansi.+ Ophedwa onsewa anali amuna ogwira lupanga.+