Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Munthu akalumbira mpaka kulankhula mosalingalira bwino,+ mwa kunena kuti achita choipa+ kapena chabwino, ngakhale kuti sanazindikire zotsatira zake, koma akadziwa kuti walankhula mosalingalira bwino pa chilichonse chimene walumbira,+ pamenepo wapalamula mlandu pa chimene walumbiracho.

  • Numeri 30:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+

  • Oweruza 21:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano amuna a Isiraeli analumbira ali ku Mizipa+ kuti: “Aliyense wa ife sadzapereka mwana wake wamkazi kuti akwatiwe ndi mwamuna wa fuko la Benjamini.”+

  • Miyambo 20:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Umakhala msampha munthu wochokera kufumbi akathamangira kufuula kuti, “N’zoyera!”+ koma pambuyo polonjeza+ n’kumafuna kuganiziranso bwino.+

  • Mlaliki 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena