Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mulungu wanga ndiye thanthwe langa.+ Ine ndidzathawira kwa iye,

      Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga+ ya chipulumutso ndi malo anga okwezeka achitetezo.+

      Iye ndi malo anga othawirako,+ Mpulumutsi wanga.+ Mumandipulumutsa ku chiwawa.+

  • Salimo 18:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+

      Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+

      Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+

  • Salimo 35:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Tengani chishango chaching’ono ndi chishango chachikulu,+

      Ndipo bwerani kuti mundithandize.+

  • Salimo 91:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+

      Udzathawira pansi pa mapiko ake.+

      Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena