Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+

      Moti anadya zokolola za m’minda.+

      Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+

      Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+

  • Yesaya 33:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+

  • Yesaya 58:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena