Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mzimu wa Yehova unandilankhulitsa,+

      Ndipo mawu ake anali palilime langa.+

  • 1 Mafumu 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Adoniya anapitiriza kuti: “Inu mukudziwa bwino kuti ufumu unayenera kukhala wanga, ndipo Aisiraeli onse maso awo anali pa ine kuti ndikhala mfumu.+ Koma ufumuwo unatembenuka n’kukhala wa m’bale wanga, chifukwa Yehova ndiye anam’patsa ufumuwo kuti ukhale wake.+

  • 1 Mafumu 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tsopano m’dzina la Yehova Mulungu wamoyo,+ amene wandichititsa kukhazikika,+ amene wandiika pampando wachifumu wa Davide bambo anga,+ ndiponso amene anandipatsa mzere wa banja lachifumu+ monga ananenera,+ lero Adoniya aphedwa.”+

  • 1 Mbiri 29:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano mfumu Davide inauza mpingo wonse+ kuti: “Solomo mwana wanga, amene Mulungu wamusankha,+ ndi wamng’ono+ ndi wosakhwima. Koma ntchitoyi ndi yaikulu chifukwa chinyumba chachikuluchi, si cha munthu ayi,+ koma ndi cha Yehova Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena