5 Pomaliza pake, Yehova anaichititsa khate mfumuyo+ moti inakhalabe yakhate+ mpaka tsiku limene inamwalira. Iyo inali kungokhala m’nyumba mwake osagwiranso ntchito.+ Pa nthawiyi, Yotamu+ mwana wa mfumuyo ndiye anali kuyang’anira nyumba ya mfumu ndi kuweruza+ anthu a m’dzikolo.