Salimo 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+ Miyambo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero anthu ochimwa amabisala kuti akhetse magazi a anthu ena.+ Amabisalira miyoyo ya anthu ena.+ Miyambo 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amene amadzikuza akapsa mtima, amatchedwa wodzikuza, wonyada ndi wodzitama.+ Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+
14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+
18 Chotero anthu ochimwa amabisala kuti akhetse magazi a anthu ena.+ Amabisalira miyoyo ya anthu ena.+