Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iyo inayamba kulankhula kwa anthuwo motsatira malangizo amene achinyamata aja+ anaipatsa. Inati: “Bambo anga anakusenzetsani goli lolemera, koma ine ndidzawonjezera goli lanulo. Bambo anga anakukwapulani ndi zikwapu, koma ine ndidzakukwapulani ndi zikoti zaminga.”+

  • Esitere 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pambuyo pake, Mfumu Ahasiwero analemekeza Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ ndipo anam’kweza+ ndi kum’patsa mpando wapamwamba kuposa akalonga ena onse amene mfumuyo inali nawo.+

  • Miyambo 28:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu olungama akamasangalala+ zimakhala bwino kwambiri, koma anthu oipa akamalamulira, munthu amadzisintha maonekedwe.+

  • Mlaliki 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena