Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Munthu woipa amakongola zinthu za ena koma osabweza,+

      Koma wolungama amakomera mtima ena ndipo amapereka mphatso.+

  • Luka 6:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Khalani opatsa ndipo inunso anthu adzakupatsani.+ Adzakhuthulira m’matumba anu muyezo wabwino, wotsendereka, wokhutchumuka ndi wosefukira. Pakuti muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.”+

  • Machitidwe 4:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ndipo onse amene anakhulupirira anakhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+ Panalibe ngakhale mmodzi wonena kuti zinthu zimene anali nazo zinali zayekha. Zonse zimene anali nazo zinali za onse.+

  • 2 Akorinto 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+

  • 1 Timoteyo 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Uwalamule kuti azichita zabwino,+ akhale olemera pa ntchito zabwino,+ owolowa manja, okonzeka kugawira ena,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena