Salimo 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+ Nyimbo ya Solomo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+ Yohane 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi+ la nyama ndi kukhala pakati pathu, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wa mwana wobadwa yekha+ kwa bambo ake. Anali wodzaza ndi kukoma mtima kwakukulu ndi choonadi.+ Aheberi 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwa chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wokongola.+ Iwo sanaope lamulo+ la mfumu.
2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+
10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+
14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi+ la nyama ndi kukhala pakati pathu, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wa mwana wobadwa yekha+ kwa bambo ake. Anali wodzaza ndi kukoma mtima kwakukulu ndi choonadi.+
23 Mwa chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wokongola.+ Iwo sanaope lamulo+ la mfumu.