2 Mafumu 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zonse zimene Yehoyakimu anachita.+ 2 Mbiri 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova Mulungu wake, ndipo sanadzichepetse+ pamaso pa mneneri+ Yeremiya+ yemwe anapita kwa iye molamulidwa ndi Yehova. 2 Mbiri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.
19 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zonse zimene Yehoyakimu anachita.+
12 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova Mulungu wake, ndipo sanadzichepetse+ pamaso pa mneneri+ Yeremiya+ yemwe anapita kwa iye molamulidwa ndi Yehova.
13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anapandukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inali itamulumbiritsa kwa Mulungu,+ ndipo anapitiriza kuumitsa khosi lake ndi mtima wake+ kuti asabwerere kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.