Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 23:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zonse zimene makolo ake anachita.+

  • 2 Mbiri 36:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova Mulungu wake, ndipo sanadzichepetse+ pamaso pa mneneri+ Yeremiya+ yemwe anapita kwa iye molamulidwa ndi Yehova.

  • Yeremiya 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Chotero mofanana ndi nkhuyu zoipa zija zimene munthu sangadye chifukwa cha kuipa kwake,+ Yehova wanena kuti: “Momwemonso ndidzapereka Zedekiya+ mfumu ya Yuda, akalonga ake ndi anthu onse opulumuka mu Yerusalemu amene atsalira m’dzikoli,+ komanso anthu okhala m’dziko la Iguputo.+

  • Yeremiya 37:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma Zedekiyayo, atumiki ake ndi anthu a m’dzikoli sanamvere mawu amene Yehova+ ananena kudzera mwa mneneri Yeremiya.+

  • Yeremiya 38:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inawayankha kuti: “Taonani! Iye ali m’manja mwanu. Palibe chimene ine mfumu ndingachite motsutsana nanu.”+

  • Ezekieli 21:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Koma iwe mtsogoleri+ wa Isiraeli, woipa ndi wovulazidwa koopsa,+ nthawi yafika yoti ulangidwe. Mapeto a zolakwa zako afika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena