Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova wanena kuti: “Kodi nsembe zanu zambirimbirizo zili ndi phindu lanji kwa ine? Nsembe zopsereza zathunthu+ za nkhosa zamphongo+ ndiponso mafuta a nyama zodyetsedwa bwino zandikwana.+ Ine sindikusangalalanso+ ndi magazi+ a ana a ng’ombe amphongo, ana a nkhosa amphongo ndiponso a mbuzi zamphongo.+

  • Yesaya 66:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Munthu amene akupha ng’ombe yamphongo ali ngati wopha munthu.+ Amene akupereka nsembe ya nkhosa ali ngati wothyola khosi la galu.+ Wopereka mphatso ali ngati wopereka magazi a nkhumba.+ Wopereka lubani wachikumbutso+ ali ngati wopereka dalitso pogwiritsa ntchito mawu onenerera zamatsenga.+ Anthuwo asankha njira zawozawo, ndipo amasangalala ndi zinthu zawo zonyansa.+

  • Amosi 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ine ndimadana ndi zikondwerero zanu ndipo ndikuzikana,+ komanso sindidzasangalala ndi fungo la nsembe zanu zoperekedwa pamisonkhano yanu yapadera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena