Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova wanena kuti: “Kodi nsembe zanu zambirimbirizo zili ndi phindu lanji kwa ine? Nsembe zopsereza zathunthu+ za nkhosa zamphongo+ ndiponso mafuta a nyama zodyetsedwa bwino zandikwana.+ Ine sindikusangalalanso+ ndi magazi+ a ana a ng’ombe amphongo, ana a nkhosa amphongo ndiponso a mbuzi zamphongo.+

  • Yeremiya 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “N’chifukwa chiyani mukundibweretsera lubani* wochokera ku Sheba+ ndi mabango onunkhira ochokera kudziko lakutali? Zimenezi zili ndi ntchito yanji kwa ine? Nsembe zanu zopsereza zathunthu sizikundisangalatsa,+ ndipo nsembe zina zonse zimene mukupereka sizikundikondweretsa.”+

  • Hoseya 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iwo anali kupereka nsembe zanyama ngati mphatso kwa ine+ ndipo anali kuzidya, koma ine Yehova sindinakondwere nazo.+ Tsopano ndidzakumbukira zolakwa zawo. Ndidzawaimba mlandu chifukwa cha machimo awo+ ndiponso chifukwa chakuti iwo anabwerera ku Iguputo.+

  • Amosi 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ine ndimadana ndi zikondwerero zanu ndipo ndikuzikana,+ komanso sindidzasangalala ndi fungo la nsembe zanu zoperekedwa pamisonkhano yanu yapadera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena