-
Zekariya 11:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho ine ndinayamba kuweta nkhosa+ zimene zinayenera kuphedwa,+ ndipo ndinachita zimenezi chifukwa cha inu, anthu osautsika a m’gulu la nkhosali.+ Chotero ndinatenga ndodo ziwiri.+ Imodzi ndinaipatsa dzina lakuti Wosangalatsa.+ Inayo ndinaipatsa dzina lakuti Mgwirizano,+ ndipo ndinayamba kuweta gulu la nkhosalo.
-