Deuteronomo 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+Moti anadya zokolola za m’minda.+Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+ Salimo 78:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Anayamba kumanga malo opatulika ngati malo okwera a paphiri,+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+ Yesaya 58:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+
13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+Moti anadya zokolola za m’minda.+Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+ Salimo 78:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Anayamba kumanga malo opatulika ngati malo okwera a paphiri,+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+ Yesaya 58:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+
69 Anayamba kumanga malo opatulika ngati malo okwera a paphiri,+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+
14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+