Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “‘Ndithu iwo adzakutonthozani mukadzaona njira zawo ndi zochita zawo. Chotero mudzadziwa kuti zonse zimene ndidzachitire mzindawo, sindinazichite popanda chifukwa,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+

  • Ezekieli 33:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Dzikolo ndikadzalisandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka+ chifukwa cha zonyansa zonse zimene achita,+ iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’

  • Danieli 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu munachitadi zimene munachenjeza kuti mudzatichitira,+ ifeyo ndi atsogoleri athu.+ Munatigwetsera tsoka lalikulu ndipo tsoka limene lagwera Yerusalemu silinachitikeponso padziko lonse lapansi.+

  • Zekariya 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kodi zimene ndinalamula atumiki anga aneneri+ m’mawu anga ndi m’malangizo anga, sizinawachitikire makolo anu?’+ Chotero iwo anabwerera kwa ine ndi kunena kuti: ‘Yehova wa makamu watichitira zimene anakonza kuti atichitire+ mogwirizana ndi njira zathu ndi zochita zathu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena