Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mudzadya chakudya cha chaka chapita,+ ndipo chimenecho mudzachitulutsa kuti mupeze malo oikapo chatsopano.

  • Miyambo 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ukatero nkhokwe zako zidzakhala zodzaza+ ndipo zoponderamo mphesa zako zidzasefukira ndi vinyo watsopano.+

  • Amosi 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika pamene wolima adzapitirira wokolola,+ ndipo woponda mphesa adzapitirira munthu amene wanyamula mbewu zoti akabzale.+ Mapiri adzachucha vinyo wotsekemera*+ ndipo zitunda zonse zidzatulutsa vinyo wochuluka.+

  • Malaki 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Bweretsani gawo limodzi mwa magawo 10 alionse a zinthu zanu+ n’kuziika mosungiramo zinthu zanga, kuti m’nyumba mwanga mukhale chakudya.+ Ndiyeseni chonde pa nkhani imeneyi,+ kuti muone ngati sindidzakutsegulirani zipata za kumwamba+ ndi kukukhuthulirani madalitso oti mudzasowa powalandirira,”+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena