-
Chivumbulutso 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma chilombocho+ chinagwidwa limodzi ndi mneneri+ wonyenga uja, amene anachita zizindikiro+ pamaso pa chilombocho. Zizindikiro zimenezi anasocheretsa nazo olandira chizindikiro+ cha chilombo ndi olambira chifaniziro chake.+ Adakali amoyo, onse awiri anaponyedwa m’nyanja ya moto yoyaka ndi sulufule.+
-
-
Chivumbulutso 20:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kenako ndinaona mipando yachifumu+ ndi amene anakhalapo. Iwo anapatsidwa mphamvu yoweruza.+ Ndiyeno ndinaona miyoyo ya amene anaphedwa ndi nkhwangwa chifukwa cha kuchitira umboni za Yesu, ndi kulankhula za Mulungu. Ndinaonanso anthu amene sanalambire chilombo+ kapena chifaniziro chake,+ ndipo sanalandire chizindikiro pamphumi pawo ndi padzanja pawo.+ Iwo anakhalanso ndi moyo ndipo analamulira monga mafumu+ limodzi ndi Khristu zaka 1,000.
-