Chivumbulutso 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuzungulira mpando wachifumuwo, panalinso mipando yachifumu yokwanira 24. Pamipando yachifumuyo,+ ndinaona patakhala akulu+ 24+ ovala malaya akunja oyera,+ ndi zisoti zachifumu+ zagolide pamitu pawo. Chivumbulutso 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo akulu+ 24 ndi zamoyo zinayi zija,+ anagwada pansi ndi kuwerama, n’kulambira Mulungu wokhala+ pampando wachifumu, ndi mawu akuti: “Ame! Tamandani Ya,+ anthu inu!”
4 Kuzungulira mpando wachifumuwo, panalinso mipando yachifumu yokwanira 24. Pamipando yachifumuyo,+ ndinaona patakhala akulu+ 24+ ovala malaya akunja oyera,+ ndi zisoti zachifumu+ zagolide pamitu pawo.
4 Ndipo akulu+ 24 ndi zamoyo zinayi zija,+ anagwada pansi ndi kuwerama, n’kulambira Mulungu wokhala+ pampando wachifumu, ndi mawu akuti: “Ame! Tamandani Ya,+ anthu inu!”