Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Angelo 7 amene anali ndi miliri 7 (1-8)

        • Nyimbo ya Mose komanso ya Mwanawankhosa (3, 4)

Chivumbulutso 15:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:1
  • +Chv 16:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 215-216

Chivumbulutso 15:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 7:23; Chv 4:6
  • +Chv 2:7
  • +Chv 13:15
  • +Chv 13:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 216-217

Chivumbulutso 15:3

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 15:1; De 31:30
  • +Yoh 1:29
  • +Eks 15:11; Sl 111:2; 139:14
  • +Eks 6:3
  • +De 32:4; Sl 145:17
  • +Yer 10:10; 1Ti 1:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Yandikirani, tsa. 12

    Zimene Baibulo Limaphunzitsa, ptsa. 13-14

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 217-218

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1996, ptsa. 14-15

Chivumbulutso 15:4

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 10:6, 7
  • +Sl 86:9; Mki 1:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Yandikirani, ptsa. 282-283

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 217-218

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1996, ptsa. 14-15

    1/1/1992, ptsa. 18-19

Chivumbulutso 15:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 7:44; Ahe 8:1, 2; 9:11
  • +Chv 11:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 218

Chivumbulutso 15:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 15:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 218-219

Chivumbulutso 15:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 75:8; Yer 25:15; Chv 14:9, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 218-219

Chivumbulutso 15:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 40:34, 35; 1Mf 8:10, 11; Yes 6:4; Eze 44:4
  • +Chv 15:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 219-220

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 15:1Chv 16:1
Chiv. 15:1Chv 16:17
Chiv. 15:21Mf 7:23; Chv 4:6
Chiv. 15:2Chv 2:7
Chiv. 15:2Chv 13:15
Chiv. 15:2Chv 13:18
Chiv. 15:3Eks 15:1; De 31:30
Chiv. 15:3Yoh 1:29
Chiv. 15:3Eks 15:11; Sl 111:2; 139:14
Chiv. 15:3Eks 6:3
Chiv. 15:3De 32:4; Sl 145:17
Chiv. 15:3Yer 10:10; 1Ti 1:17
Chiv. 15:4Yer 10:6, 7
Chiv. 15:4Sl 86:9; Mki 1:11
Chiv. 15:5Mac 7:44; Ahe 8:1, 2; 9:11
Chiv. 15:5Chv 11:19
Chiv. 15:6Chv 15:1
Chiv. 15:7Sl 75:8; Yer 25:15; Chv 14:9, 10
Chiv. 15:8Eks 40:34, 35; 1Mf 8:10, 11; Yes 6:4; Eze 44:4
Chiv. 15:8Chv 15:1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 15:1-8

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

15 Ndinaona chizindikiro china kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Chizindikiro chimenechi chinali angelo 7+ amene anali ndi miliri 7. Miliri imeneyi ndi yomaliza chifukwa ikamatha, mkwiyo wa Mulungu udzakhalanso utatha.+

2 Kenako ndinaona chinachake chooneka ngati nyanja yagalasi+ yosakanikirana ndi moto. Ndipo amene anagonjetsa+ chilombo chija, chifaniziro chake+ ndi nambala ya dzina lake+ anali ataima pambali pa nyanja yagalasiyo, atanyamula azeze a Mulungu. 3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti:

“Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+ 4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”

5 Zimenezi zitatha, ndinaona malo opatulika amʼchihema cha umboni+ atatsegulidwa kumwamba.+ 6 Ndipo angelo 7 amene anali ndi miliri 7+ aja anatuluka kumalo opatulikawo, atavala zovala zoyera ndi zowala komanso atamanga malamba agolide pazifuwa zawo. 7 Ndiyeno mmodzi wa angelo 4 aja anapereka kwa angelo 7 amenewo mbale zagolide 7 zodzaza ndi mkwiyo wa Mulungu,+ amene adzakhala ndi moyo mpaka kalekale. 8 Mʼmalo opatulikawo munadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa mʼmalo opatulikawo mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena