Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 15:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Sauli anayankha Samueli kuti: “Komatu ndamvera+ mawu a Yehova, chifukwa ndachita ntchito imene Yehova anandituma, ndipo ndabweretsa Agagi,+ mfumu ya Amaleki. Koma Aamalekiwo ndawapha.+

  • Esitere 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pambuyo pake, Mfumu Ahasiwero analemekeza Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ ndipo anam’kweza+ ndi kum’patsa mpando wapamwamba kuposa akalonga ena onse amene mfumuyo inali nawo.+

  • Esitere 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha.

  • Esitere 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Izi zinali choncho chifukwa Hamani+ mwana wa Hamedata+ Mwagagi,+ amene anali kudana+ ndi Ayuda onse, anakonzera Ayudawo chiwembu kuti awawononge.+ Choncho iye anachita Puri+ kapena kuti Maere,+ ndi cholinga chakuti awasautse ndi kuwawononga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena