Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 85:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Ndithudi, chipulumutso chake chili pafupi ndi amene amamuopa,+

      Kuti ulemerero ukhale m’dziko lathu.+

  • Miyambo 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Nzeru ndi malangizo zimanyozedwa ndi zitsiru.*+

  • Miyambo 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kuopa Yehova ndiko chitsime cha moyo,+ chifukwa kumateteza moyo kumisampha ya imfa.+

  • Malaki 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pa nthawi imeneyo anthu oopa Yehova+ analankhulana, aliyense ndi mnzake, ndipo Yehova anatchera khutu ndi kumvetsera.+ Buku la chikumbutso linayamba kulembedwa pamaso pake.+ Buku limeneli linali lonena za anthu oopa Yehova ndi anthu amene anali kuganizira za dzina lake.+

  • Machitidwe 9:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pamenepo mpingo+ mu Yudeya monse, mu Galileya, ndi mu Samariya unalowa m’nyengo yamtendere, ndipo unakhala wolimba. Popeza kuti unali kuyenda moopa Yehova+ ndiponso kulimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unali kukulirakulira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena