Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako Sauli anatumiza amithenga+ kunyumba ya Davide kuti akaizungulire ndi kupha Davide m’mawa mwa tsiku limenelo.+ Koma Mikala mkazi wa Davide anauza Davideyo kuti: “Ngati supulumutsa moyo wako usiku uno, mawa ukhala utaphedwa.”

  • Salimo 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye amabisalira anthu pafupi ndi midzi.

      Amabisalira munthu wosalakwa ndi kumupha.+

      ע [ʽAʹyin]

      Maso ake amafunafuna waumphawi.+

  • Salimo 37:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Woipa amalondalonda munthu wolungama,+

      Ndipo amafuna kuti amuphe.+

  • Salimo 56:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Amandiukira ndi kundibisalira,+

      Iwo nthawi zonse amaonetsetsa mmene ndikuyendera,+

      Pamene akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+

  • Miyambo 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Akamanena kuti: “Tiye tipitire limodzi. Tiye tikabisalire anthu kuti tikakhetse magazi.+ Tiye tikabisalire anthu osalakwa. Tikachite zimenezo popanda chifukwa chilichonse.+

  • Mateyu 26:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena