Salimo 61:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti inu Mulungu, mwamvetsera malonjezo anga.+Mwandipatsa cholowa chimene mwasungira anthu oopa dzina lanu.+ Yesaya 58:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+
5 Pakuti inu Mulungu, mwamvetsera malonjezo anga.+Mwandipatsa cholowa chimene mwasungira anthu oopa dzina lanu.+
14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+