-
Danieli 9:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 “Pambuyo pa milungu 62 imeneyi, Mesiya adzaphedwa+ ndipo sadzasiya kalikonse.+
“Gulu lankhondo la mtsogoleri amene akubwera lidzawononga+ mzindawo ndi malo oyera.+ Malo oyera amenewo adzafafanizidwa ndi madzi osefukira, ndipo padzakhala nkhondo mpaka kumapeto. Mulungu wagamula kuti padzakhale chiwonongeko.+
-
-
Luka 22:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno anawauza kuti: “Ndinali wofunitsitsa kudya pasika uyu limodzi ndi inu ndisanalowe m’masautso.
-