Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 13
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 13:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 5:22
  • +Chv 11:7; 13:18; 19:20
  • +Yes 57:20; Da 7:2; Hab 1:14; Chv 17:15; 21:1
  • +Da 7:7
  • +Chv 13:3
  • +Sl 74:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2012, ptsa. 8-11, 14-18

    2/15/2009, tsa. 4

    4/1/2004, tsa. 4

    4/1/1989, tsa. 20

    12/15/1988, tsa. 19

    2/1/1986, ptsa. 5-6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 186-190

Chivumbulutso 13:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:6
  • +Da 7:5
  • +Da 7:4
  • +Chv 12:9
  • +Lu 4:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2022, tsa. 15

    5/2022, tsa. 9

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 186-188, 189-190, 227

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/2004, tsa. 4

    7/15/1990, tsa. 30

    12/15/1988, tsa. 19

    2/1/1986, ptsa. 5-6

    Kukambitsirana, tsa. 129

Chivumbulutso 13:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 190-191

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 13:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 191-192

Chivumbulutso 13:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:8
  • +Lu 12:10
  • +Chv 11:2, 3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 192

Chivumbulutso 13:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 5:2; Yes 14:13; Da 7:25
  • +Chv 12:12

Chivumbulutso 13:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 19:11
  • +Lu 22:31; Chv 12:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2012, tsa. 15

    2/1/1986, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 192

Chivumbulutso 13:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 12:1; Chv 3:5; 21:27
  • +Yes 53:7; Mt 27:50; Chv 5:6, 12
  • +Aef 1:4; 1Pe 1:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 3

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 192

Chivumbulutso 13:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 11:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 192-193

Chivumbulutso 13:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zek 14:2
  • +Ge 9:6; Mt 26:52
  • +Da 7:18; 1Ak 6:2; Chv 20:6
  • +Mt 24:13; Ahe 10:36; 12:3
  • +Chv 2:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 192-193

Chivumbulutso 13:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:8; Chv 16:13; 19:20
  • +Chv 12:16
  • +Da 7:8; Chv 16:13; 20:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, ptsa. 3-4

    4/1/1989, tsa. 20

    5/15/1988, ptsa. 25-26

    2/1/1986, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 193-194

Chivumbulutso 13:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:1
  • +Chv 13:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 193-194

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/1986, tsa. 6

Chivumbulutso 13:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 13:1; Mt 24:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, ptsa. 3-4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 193-194

Chivumbulutso 13:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 20:4; Chv 19:20; 20:4
  • +Chv 13:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 194-195, 240-241

    Galamukani!,

    12/8/1990, tsa. 28

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1989, tsa. 20

    6/1/1988, ptsa. 25-26

    2/1/1986, ptsa. 6-7

Chivumbulutso 13:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 29:17; 1Mf 11:5; Da 3:6; Mt 24:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 194-195, 240-241

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 13:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 39:10; 52:16
  • +Chv 14:9; 16:2; 19:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2021, tsa. 18

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    4/1/2004, ptsa. 6-7

    11/1/1997, ptsa. 15-16

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 195-198

Chivumbulutso 13:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 14:11
  • +Chv 15:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    11/1/1997, ptsa. 15-16

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 195-198

Chivumbulutso 13:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mla 7:20; Aro 3:23
  • +1Mb 20:6; Da 3:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    4/1/2004, ptsa. 3, 4-7

    12/15/1988, ptsa. 19-20

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 195-196

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 13:1Yer 5:22
Chiv. 13:1Chv 11:7; 13:18; 19:20
Chiv. 13:1Yes 57:20; Da 7:2; Hab 1:14; Chv 17:15; 21:1
Chiv. 13:1Da 7:7
Chiv. 13:1Chv 13:3
Chiv. 13:1Sl 74:10
Chiv. 13:2Da 7:6
Chiv. 13:2Da 7:5
Chiv. 13:2Da 7:4
Chiv. 13:2Chv 12:9
Chiv. 13:2Lu 4:6
Chiv. 13:3Chv 13:14
Chiv. 13:5Da 7:8
Chiv. 13:5Lu 12:10
Chiv. 13:5Chv 11:2, 3
Chiv. 13:6Eks 5:2; Yes 14:13; Da 7:25
Chiv. 13:6Chv 12:12
Chiv. 13:7Yoh 19:11
Chiv. 13:7Lu 22:31; Chv 12:17
Chiv. 13:8Da 12:1; Chv 3:5; 21:27
Chiv. 13:8Yes 53:7; Mt 27:50; Chv 5:6, 12
Chiv. 13:8Aef 1:4; 1Pe 1:20
Chiv. 13:9Mt 11:15
Chiv. 13:10Zek 14:2
Chiv. 13:10Ge 9:6; Mt 26:52
Chiv. 13:10Da 7:18; 1Ak 6:2; Chv 20:6
Chiv. 13:10Mt 24:13; Ahe 10:36; 12:3
Chiv. 13:10Chv 2:10
Chiv. 13:11Da 7:8; Chv 16:13; 19:20
Chiv. 13:11Chv 12:16
Chiv. 13:11Da 7:8; Chv 16:13; 20:2
Chiv. 13:12Chv 13:1
Chiv. 13:12Chv 13:3
Chiv. 13:13De 13:1; Mt 24:24
Chiv. 13:14Eks 20:4; Chv 19:20; 20:4
Chiv. 13:14Chv 13:3
Chiv. 13:15De 29:17; 1Mf 11:5; Da 3:6; Mt 24:15
Chiv. 13:16Yer 39:10; 52:16
Chiv. 13:16Chv 14:9; 16:2; 19:20
Chiv. 13:17Chv 14:11
Chiv. 13:17Chv 15:2
Chiv. 13:18Mla 7:20; Aro 3:23
Chiv. 13:181Mb 20:6; Da 3:1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 13:1-18

Chivumbulutso

13 Ndiyeno chinjokacho chinangoima pamchenga+ wa m’mbali mwa nyanja.

Kenako ndinaona chilombo+ chikutuluka m’nyanja.+ Chinali ndi nyanga 10+ ndi mitu 7.+ Kunyanga yake iliyonse kunali chisoti chachifumu. Koma pamitu yake panali mayina onyoza Mulungu.+ 2 Chilombo chimene ndinaonacho chinali ngati nyalugwe,+ koma mapazi ake anali ngati a chimbalangondo,+ ndipo pakamwa pake panali ngati pa mkango.+ Chinjoka+ chija chinapatsa chilombocho mphamvu yake, mpando wake wachifumu, komanso ulamuliro wake waukulu.+

3 Ndiyeno ndinaona mutu wake umodzi ukuoneka kuti wavulazidwa kwambiri. Koma ngakhale kuti balalo linali loti chikanafa nalo,+ linapola. Ndipo dziko lonse lapansi linatsatira chilombocho pochita nacho chidwi. 4 Iwo analambira chinjoka chija chifukwa chinapatsa chilombo ulamuliro. Ndipo analambira chilombocho ndi mawu awa: “Ndani ali ngati chilombo, ndipo ndani angamenyane nacho?” 5 Chilombocho chinapatsidwa pakamwa polankhula zinthu zodzitukumula+ ndi zonyoza.+ Chinapatsidwanso mphamvu yochita ulamuliro kwa miyezi 42.+ 6 Chilombocho chinatsegula pakamwa pake n’kumanyoza Mulungu,+ dzina lake ndi malo ake okhala, ndiponso amene akukhala kumwamba.+ 7 Chinaloledwa+ kuchita nkhondo ndi oyerawo ndi kuwagonjetsa.+ Chinapatsidwanso ulamuliro pa anthu a fuko lililonse, mtundu uliwonse, chinenero chilichonse ndi dziko lililonse. 8 Ndipo onse okhala padziko lapansi adzachilambira. Anthu onsewa mayina awo sanalembedwe mumpukutu+ wa moyo, umene Mwanawankhosa amene anaphedwa,+ ndiye mwiniwake. Mpukutuwo unakonzedwa kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+

9 Aliyense amene ali ndi makutu amve.+ 10 Ngati wina akuyenera kutengedwa ukapolo, adzapitadi ku ukapoloko.+ Ngati wina adzapha ndi lupanga, adzaphedwa ndi lupanga.+ Apa m’pamene oyera+ akufunika kupirira+ ndiponso kukhala ndi chikhulupiriro.+

11 Kenako ndinaona chilombo+ china chikutuluka pansi pa dziko lapansi.+ Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+ 12 Chilombocho chinalamulira ndi mphamvu zonse za chilombo choyambacho+ pamaso pa chilombo choyambacho. Chinachititsa dziko lapansi ndi okhalamo kulambira chilombo choyamba chija, chimene bala lake limene chinayenera kufa nalo, linapola.+ 13 Chinachitanso zizindikiro zazikulu,+ moti chinapangitsa ngakhale moto kugwera padziko lapansi kuchokera kumwamba, anthu akuona.

14 Chilombocho chinasocheretsa okhala padziko lapansi chifukwa cha zizindikiro zimene chinaloledwa kuchita pamaso pa chilombo choyamba chija. Ndipo chinauza okhala padziko lapansi kupanga chifaniziro+ cha chilombo chimene chinali ndi bala la lupanga+ chija, koma chimene chinapulumuka. 15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya ku chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula, ndi kuchititsa kuti onse amene mwa njira iliyonse salambira chifaniziro+ cha chilombocho, aphedwe.

16 Chilombocho chinakakamiza anthu onse,+ olemekezeka ndi onyozeka, olemera ndi osauka, mfulu ndi akapolo, kuti apatsidwe chizindikiro padzanja lawo lamanja kapena pamphumi pawo.+ 17 Chinachita izi kuti aliyense asathe kugula kapena kugulitsa, kupatulapo ngati ali ndi chizindikirocho, dzina+ la chilombo, kapena nambala ya dzina lake.+ 18 Apa ndiye pofunika nzeru: Amene ali ndi nzeru awerengere nambala ya chilombocho, pakuti ndi nambala ya munthu.+ Nambala yake ndi 666.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena