Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Katatu pa chaka muzindichitira chikondwerero.+

  • 1 Samueli 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chaka chilichonse mwamuna ameneyu ankachoka mumzinda wawo nʼkupita ku Silo, kukalambira* Yehova wa magulu ankhondo akumwamba komanso kukapereka nsembe zake.+ Kumeneko nʼkumene ana awiri a Eli, Hofeni ndi Pinihasi,+ ankatumikira monga ansembe a Yehova.+

  • 1 Samueli 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Patapita nthawi, Elikana anapita ndi banja lake lonse kukapereka kwa Yehova nsembe yapachaka+ ndi nsembe yake yalonjezo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena