Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 17:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 ndipo anati: “Popeza dzanja laukira mpando wachifumu+ wa Ya,+ Yehova adzamenya nkhondo ndi Aamaleki ku mibadwomibadwo.”+

  • Numeri 24:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+

      “Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+

      Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+

  • Deuteronomo 25:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.

  • 1 Samueli 15:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Sauli anayankha Samueli kuti: “Komatu ndamvera+ mawu a Yehova, chifukwa ndachita ntchito imene Yehova anandituma, ndipo ndabweretsa Agagi,+ mfumu ya Amaleki. Koma Aamalekiwo ndawapha.+

  • 1 Samueli 30:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, pamene Davide ndi asilikali ake anali kubwerera ku Zikilaga+ tsiku lachitatu, Aamaleki+ anaukira anthu a kum’mwera* ndi a mumzinda wa Zikilaga ndi kufunkha zinthu zawo. Iwo anathira nkhondo mzindawo ndi kuutentha ndi moto.

  • 1 Samueli 30:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Davide analanditsa zonse zimene Aamaleki anatenga,+ n’kulanditsanso akazi ake awiri aja.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena