Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+

      Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+

      Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+

      Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+

      Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+

  • Salimo 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+

      Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+

      Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+

  • Luka 17:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndipo anthu sadzanena kuti, ‘Onani kuno!’ kapena, ‘Uko!’+ Pakuti ufumu wa Mulungu uli pakati panu.”+

  • Yohane 1:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Choyamba iyeyu anapeza m’bale wake Simoni, ndi kumuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina lotanthauza, Khristu,+ polimasulira).

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena