Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 6
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 6:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:6
  • +Chv 5:5
  • +Chv 4:7
  • +Chv 22:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 89-90

Chivumbulutso 6:2

Mawu a M'munsi

  • *

    Ena amati “hosi” kapena “kavalo.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 39:25; Miy 21:31; Chv 19:11
  • +Sl 45:4
  • +2Mf 9:24
  • +Ge 49:10; Sl 21:3; Eze 21:27; Da 7:14; Chv 14:14
  • +Sl 110:2; Chv 12:7
  • +Chv 16:14; 17:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    11/2019, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 4, 6, 8

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2014, ptsa. 5, 7

    2/1/2014, tsa. 6

    9/15/2010, tsa. 29

    4/15/2009, tsa. 30

    1/15/2005, tsa. 17

    6/1/2001, ptsa. 17-22

    10/15/1988, ptsa. 10-11, 15-16

    1/15/1986, ptsa. 3, 6

    1/1/1986, ptsa. 3, 4-6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 90-93

    Galamukani!,

    5/8/1988, ptsa. 14-16

Chivumbulutso 6:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 93

Chivumbulutso 6:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 11:40; Mt 24:7; Lu 21:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2014, tsa. 6

    9/1/2005, ptsa. 19-20

    9/15/1998, tsa. 7

    3/1/1993, ptsa. 4-5

    1/15/1986, ptsa. 3-4

    1/1/1986, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 93-95

    Mawu a Mulungu, ptsa. 137-139

    Galamukani!,

    5/8/1988, ptsa. 3, 5-6, 7-9

    3/8/1988, ptsa. 15-16

    Mtendere Weniweni, ptsa. 10, 11-12

Chivumbulutso 6:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:1
  • +Chv 4:7
  • +Eze 4:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 5, 7

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2014, tsa. 7

    1/15/1986, ptsa. 3-5

    1/1/1986, ptsa. 6-7

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 95

    Mawu a Mulungu, ptsa. 139-141

    Galamukani!,

    5/8/1988, ptsa. 3, 9-10

Chivumbulutso 6:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:6
  • +Chv 7:11
  • +Mt 20:2
  • +Mko 13:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 5, 7

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 96

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/1998, tsa. 7

    8/1/1995, tsa. 4

    1/15/1986, ptsa. 3-5

    Mawu a Mulungu, ptsa. 139-141

Chivumbulutso 6:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 96

Chivumbulutso 6:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 20:13
  • +Yer 15:3; Amo 4:10
  • +Yer 15:2; Eze 5:17; Lu 21:11
  • +Le 26:22; Eze 14:21; 33:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 5, 7

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2014, tsa. 7

    5/1/2005, tsa. 17

    5/15/1993, tsa. 31

    10/15/1988, ptsa. 11-12

    1/15/1986, ptsa. 3, 5

    1/1/1986, tsa. 7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 96-98

    Galamukani!,

    10/8/1994, tsa. 30

    5/8/1988, ptsa. 3, 10-11

    Mawu a Mulungu, ptsa. 142-146

    Mtendere Weniweni, ptsa. 14-15

Chivumbulutso 6:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Le 4:7; Chv 8:3
  • +Le 17:11; Chv 17:6
  • +Mt 24:9; 1Yo 3:12
  • +Mt 24:14; Yoh 18:37; Chv 20:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, ptsa. 28-29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 100, 289

Chivumbulutso 6:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 4:24
  • +1Yo 5:20
  • +Lu 18:7; Ahe 12:23; Chv 19:2
  • +Ge 4:10; De 32:43

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 101-102, 245, 289

Chivumbulutso 6:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:5; 4:4
  • +Mt 24:9; Mac 9:1; 2Ak 1:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, ptsa. 29-30

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 102-104, 289

Chivumbulutso 6:12

Mawu a M'munsi

  • *

    Ena amati “saka.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 50:3
  • +Yow 2:31; Mt 24:29; Mac 2:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 104-110

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, tsa. 17

Chivumbulutso 6:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 109-110

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, tsa. 17

Chivumbulutso 6:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 34:4
  • +Chv 16:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    4/2017, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 110-112

Chivumbulutso 6:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 2:10, 19; Eze 33:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 16

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 112

Chivumbulutso 6:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ho 10:8; Lu 23:30
  • +Chv 4:2
  • +Chv 5:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 112

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1997, tsa. 20

Chivumbulutso 6:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zef 1:14
  • +Zef 1:18; Aro 2:5
  • +Yow 2:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2014, tsa. 31

    12/15/1988, ptsa. 11-12

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 112-113, 128-129

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 6:1Chv 5:6
Chiv. 6:1Chv 5:5
Chiv. 6:1Chv 4:7
Chiv. 6:1Chv 22:20
Chiv. 6:2Yob 39:25; Miy 21:31; Chv 19:11
Chiv. 6:2Sl 45:4
Chiv. 6:22Mf 9:24
Chiv. 6:2Ge 49:10; Sl 21:3; Eze 21:27; Da 7:14; Chv 14:14
Chiv. 6:2Sl 110:2; Chv 12:7
Chiv. 6:2Chv 16:14; 17:14
Chiv. 6:3Chv 4:7
Chiv. 6:4Da 11:40; Mt 24:7; Lu 21:10
Chiv. 6:5Chv 6:1
Chiv. 6:5Chv 4:7
Chiv. 6:5Eze 4:16
Chiv. 6:6Chv 5:6
Chiv. 6:6Chv 7:11
Chiv. 6:6Mt 20:2
Chiv. 6:6Mko 13:8
Chiv. 6:7Chv 4:7
Chiv. 6:8Chv 20:13
Chiv. 6:8Yer 15:3; Amo 4:10
Chiv. 6:8Yer 15:2; Eze 5:17; Lu 21:11
Chiv. 6:8Le 26:22; Eze 14:21; 33:27
Chiv. 6:9Le 4:7; Chv 8:3
Chiv. 6:9Le 17:11; Chv 17:6
Chiv. 6:9Mt 24:9; 1Yo 3:12
Chiv. 6:9Mt 24:14; Yoh 18:37; Chv 20:4
Chiv. 6:10Mac 4:24
Chiv. 6:101Yo 5:20
Chiv. 6:10Lu 18:7; Ahe 12:23; Chv 19:2
Chiv. 6:10Ge 4:10; De 32:43
Chiv. 6:11Chv 3:5; 4:4
Chiv. 6:11Mt 24:9; Mac 9:1; 2Ak 1:8
Chiv. 6:12Yes 50:3
Chiv. 6:12Yow 2:31; Mt 24:29; Mac 2:20
Chiv. 6:14Yes 34:4
Chiv. 6:14Chv 16:20
Chiv. 6:15Yes 2:10, 19; Eze 33:27
Chiv. 6:16Ho 10:8; Lu 23:30
Chiv. 6:16Chv 4:2
Chiv. 6:16Chv 5:6
Chiv. 6:17Zef 1:14
Chiv. 6:17Zef 1:18; Aro 2:5
Chiv. 6:17Yow 2:11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 6:1-17

Chivumbulutso

6 Ndinaona Mwanawankhosa+ atamatula chidindo chimodzi mwa zidindo 7 zija,+ ndipo ndinamva chamoyo chimodzi mwa zamoyo zinayi zija+ chikulankhula ndi mawu ngati kugunda kwa bingu kuti: “Bwera!”+ 2 Nditayang’ana, ndinaona hatchi* yoyera.+ Wokwerapo+ wake ananyamula uta.+ Iye anapatsidwa chisoti chachifumu,+ ndi kupita kukagonjetsa adani ake+ ndipo anapambana pa nkhondo yolimbana nawo.+

3 Atamatula chidindo chachiwiri, ndinamva chamoyo chachiwiri+ chikunena kuti: “Bwera!” 4 Pamenepo, hatchi ina inatulukira. Imeneyi inali yofiira ngati moto. Wokwerapo wake analoledwa kuchotsa mtendere padziko lapansi, kuti anthu aphane. Iye anapatsidwanso lupanga lalikulu.+

5 Atamatula+ chidindo chachitatu, ndinamva chamoyo chachitatu+ chikunena kuti: “Bwera!” Ndipo nditayang’ana, ndinaona hatchi yakuda. Wokwerapo wake anali ndi sikelo+ m’dzanja lake. 6 Kenako ndinamva mawu ngati ochokera pakati+ pa zamoyo zinayi zija.+ Mawuwo anali akuti: “Kilogalamu imodzi ya tirigu, mtengo wake ukhala dinari imodzi,+ ndipo makilogalamu atatu a balere, mtengo wake ukhala dinari imodzi. Koma musawononge mafuta a maolivi ndi vinyo.”+

7 Atamatula chidindo chachinayi, ndinamva mawu a chamoyo chachinayi+ chikunena kuti: “Bwera!” 8 Nditayang’ana, ndinaona hatchi yotuwa. Wokwerapo wake dzina lake anali Imfa. Ndipo Manda+ anali kumutsatira pafupi kwambiri. Iwo anapatsidwa ulamuliro pa gawo limodzi la magawo anayi a dziko lapansi, kuti aphe anthu ndi lupanga lalitali,+ njala,+ mliri wakupha, ndi zilombo+ za padziko lapansi.

9 Atamatula chidindo chachisanu, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo+ ya amene anaphedwa+ chifukwa cha mawu a Mulungu, ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni+ imene anali nayo. 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera kufikira liti, Inu Ambuye Wamkulu Koposa,+ woyera ndi woona,+ osaweruza+ ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi+ athu?” 11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera,+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pang’ono, kufikira chitakwanira chiwerengero cha akapolo anzawo, ndi abale awo amene anali pafupi kuphedwa+ monga mmene iwonso anaphedwera.

12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli*+ choluka ndi ubweya wa mbuzi yakuda, ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+ 13 Nyenyezi zakumwamba zinagwera kudziko lapansi, ngati mmene mkuyu wogwedezeka ndi mphepo yamphamvu umagwetsera nkhuyu zake zosapsa. 14 Ndipo kumwamba kunakanganuka ngati mpukutu umene akuupinda,+ ndipo phiri lililonse ndi chilumba chilichonse zinachotsedwa m’malo awo.+ 15 Mafumu a dziko lapansi, nduna, akuluakulu a asilikali, olemera, amphamvu, kapolo aliyense ndi mfulu aliyense, anabisala m’mapanga ndi m’matanthwe+ a m’mapiri. 16 Iwo anali kuuza mapiri ndi matanthwe mosalekeza kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Iye amene wakhala pampando wachifumu,+ ndiponso kuti tibisike ku mkwiyo wa Mwanawankhosa,+ 17 chifukwa tsiku lalikulu+ la mkwiyo wawo+ lafika, ndipo ndani angaimirire pamaso pawo?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena