Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 3
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 3:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:1
  • +Chv 1:4; 4:5
  • +Chv 1:16
  • +Yak 2:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 3-4

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    5/15/2003, ptsa. 16-17

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 30, 54-55

Chivumbulutso 3:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 21:34; Aef 5:15; 1At 5:6
  • +Lu 22:32; Mac 18:23
  • +2Ak 6:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 3-4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 55-56

Chivumbulutso 3:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 10:8
  • +Lu 21:36; Afi 2:16
  • +Mt 3:8; 2Ak 7:11
  • +Aef 5:14
  • +Chv 16:15
  • +Mt 24:42; Lu 12:39

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 3-4

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/2009, ptsa. 13-14

    5/15/2003, tsa. 17

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 31-32, 55-56

Chivumbulutso 3:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 10:7; 22:1; Mla 7:1
  • +Yak 1:27
  • +Chv 3:18; 6:11
  • +Aef 4:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 56-58

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 17

Chivumbulutso 3:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 5:4
  • +Chv 4:4; 19:8
  • +Afi 4:3; Chv 21:27
  • +Mt 10:32; Mko 8:38
  • +Lu 12:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2012, tsa. 15

    5/15/2003, tsa. 17

    9/1/1987, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 56-58, 102-103

Chivumbulutso 3:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 4:2

Chivumbulutso 3:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:1
  • +Yoh 6:69; Mac 3:14; Ahe 7:26
  • +Chv 3:14; 19:11
  • +Yes 22:22; Lu 1:32

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 31

    5/15/2003, tsa. 17

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 58-60, 63

Chivumbulutso 3:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:2
  • +1Ak 16:9; 2Ak 2:12
  • +Mt 25:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 60-61, 62-65

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 17

    4/1/1989, tsa. 12

Chivumbulutso 3:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 8:44
  • +Aro 2:28; Chv 2:9
  • +Yes 60:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 60-62, 63-64

Chivumbulutso 3:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 8:15; 21:19; 2Ti 2:12; Ahe 10:36; 12:3
  • +2At 3:3; 2Pe 2:9
  • +Mt 24:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 31-32, 61-62

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, ptsa. 17-18

    12/1/1999, ptsa. 16-17

Chivumbulutso 3:11

Mawu a M'munsi

  • *

    Mawu ake enieni, “chisoti chachitsulo chooneka ngati nkhata.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:16
  • +Chv 2:10
  • +Yak 1:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2012, tsa. 21

    5/15/2003, ptsa. 17-18

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 61

Chivumbulutso 3:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Mb 3:17
  • +1Ak 3:16; Aef 2:21; 1Pe 2:5
  • +Mt 27:46; Yoh 20:17
  • +Ahe 12:22; Chv 21:2
  • +Chv 14:1; 19:12; 22:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 31

    5/15/2003, ptsa. 18-19

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 64-65, 280-281, 292-293

Chivumbulutso 3:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 4:2

Chivumbulutso 3:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 4:16
  • +2Ak 1:20
  • +Yoh 18:37; 1Ti 6:13
  • +Ahe 3:6; Chv 1:5
  • +Yoh 1:14; Chv 19:11
  • +Miy 8:22; Akl 1:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2009, tsa. 27

    12/15/2008, tsa. 13

    5/15/2003, tsa. 19

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 66-67

    Kukambitsirana, tsa. 395

Chivumbulutso 3:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 66-67

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 19

    4/1/1989, tsa. 13

Chivumbulutso 3:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 69:9; 2Ak 9:2
  • +Miy 25:13, 25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 66-67

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 19

Chivumbulutso 3:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ho 12:8; 1Ak 4:8
  • +2Pe 1:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 4

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, ptsa. 27-28

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2006, tsa. 22

    4/1/1989, tsa. 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 67-68

Chivumbulutso 3:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 23:10; 1Pe 1:7
  • +Chv 16:15
  • +Sl 19:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 31

    3/15/2007, tsa. 14

    5/15/2003, tsa. 19

    10/1/2002, ptsa. 21-22

    12/15/2001, tsa. 32

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 68-71

Chivumbulutso 3:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 3:12
  • +Chv 2:5; 3:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 71

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 19

Chivumbulutso 3:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yak 5:9
  • +Lu 12:36

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 71-72

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 3:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 5:4; Chv 2:26; 12:11
  • +Mt 19:28; Lu 22:30
  • +Ahe 10:12
  • +Yes 66:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 72-73

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 20

Chivumbulutso 3:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:7
  • +Chv 1:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 73

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1989, tsa. 14

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 3:1Chv 2:1
Chiv. 3:1Chv 1:4; 4:5
Chiv. 3:1Chv 1:16
Chiv. 3:1Yak 2:26
Chiv. 3:2Lu 21:34; Aef 5:15; 1At 5:6
Chiv. 3:2Lu 22:32; Mac 18:23
Chiv. 3:22Ak 6:1
Chiv. 3:3Mt 10:8
Chiv. 3:3Lu 21:36; Afi 2:16
Chiv. 3:3Mt 3:8; 2Ak 7:11
Chiv. 3:3Aef 5:14
Chiv. 3:3Chv 16:15
Chiv. 3:3Mt 24:42; Lu 12:39
Chiv. 3:4Miy 10:7; 22:1; Mla 7:1
Chiv. 3:4Yak 1:27
Chiv. 3:4Chv 3:18; 6:11
Chiv. 3:4Aef 4:1
Chiv. 3:51Yo 5:4
Chiv. 3:5Chv 4:4; 19:8
Chiv. 3:5Afi 4:3; Chv 21:27
Chiv. 3:5Mt 10:32; Mko 8:38
Chiv. 3:5Lu 12:8
Chiv. 3:61Yo 4:2
Chiv. 3:7Chv 2:1
Chiv. 3:7Yoh 6:69; Mac 3:14; Ahe 7:26
Chiv. 3:7Chv 3:14; 19:11
Chiv. 3:7Yes 22:22; Lu 1:32
Chiv. 3:8Chv 2:2
Chiv. 3:81Ak 16:9; 2Ak 2:12
Chiv. 3:8Mt 25:21
Chiv. 3:9Yoh 8:44
Chiv. 3:9Aro 2:28; Chv 2:9
Chiv. 3:9Yes 60:14
Chiv. 3:10Lu 8:15; 21:19; 2Ti 2:12; Ahe 10:36; 12:3
Chiv. 3:102At 3:3; 2Pe 2:9
Chiv. 3:10Mt 24:21
Chiv. 3:11Chv 2:16
Chiv. 3:11Chv 2:10
Chiv. 3:11Yak 1:12
Chiv. 3:122Mb 3:17
Chiv. 3:121Ak 3:16; Aef 2:21; 1Pe 2:5
Chiv. 3:12Mt 27:46; Yoh 20:17
Chiv. 3:12Ahe 12:22; Chv 21:2
Chiv. 3:12Chv 14:1; 19:12; 22:4
Chiv. 3:131Yo 4:2
Chiv. 3:14Akl 4:16
Chiv. 3:142Ak 1:20
Chiv. 3:14Yoh 18:37; 1Ti 6:13
Chiv. 3:14Ahe 3:6; Chv 1:5
Chiv. 3:14Yoh 1:14; Chv 19:11
Chiv. 3:14Miy 8:22; Akl 1:15
Chiv. 3:16Sl 69:9; 2Ak 9:2
Chiv. 3:16Miy 25:13, 25
Chiv. 3:17Ho 12:8; 1Ak 4:8
Chiv. 3:172Pe 1:9
Chiv. 3:18Yob 23:10; 1Pe 1:7
Chiv. 3:18Chv 16:15
Chiv. 3:18Sl 19:8
Chiv. 3:19Miy 3:12
Chiv. 3:19Chv 2:5; 3:3
Chiv. 3:20Yak 5:9
Chiv. 3:20Lu 12:36
Chiv. 3:211Yo 5:4; Chv 2:26; 12:11
Chiv. 3:21Mt 19:28; Lu 22:30
Chiv. 3:21Ahe 10:12
Chiv. 3:21Yes 66:1
Chiv. 3:22Chv 2:7
Chiv. 3:22Chv 1:11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 3:1-22

Chivumbulutso

3 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Sade, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena iye amene ali ndi mizimu 7+ ya Mulungu, ndi nyenyezi 7.+ ‘Ndikudziwa ntchito zako, kuti uli ndi dzina lakuti uli moyo, pamene ndiwe wakufa.+ 2 Khala maso,+ ndipo limbikitsa+ otsala amene atsala pang’ono kufa, chifukwa ndapeza kuti ntchito zako sizinachitidwe mokwanira pamaso pa Mulungu wanga.+ 3 Choncho, pitiriza kukumbukira zimene unalandira+ ndi zimene unamva. Pitiriza kuzitsatira,+ ndipo ulape.+ Ndithudi, ukapanda kudzuka,+ ndidzabwera ngati mbala,+ ndipo sudzadziwa ngakhale pang’ono ola limene ndidzafike kwa iwe.+

4 “‘Ngakhale zili choncho, uli ndi mayina+ angapo mu Sade a anthu amene sanaipitse+ malaya awo akunja. Amenewa adzayenda ndi ine atavala malaya oyera,+ chifukwa ndi oyenerera.+ 5 Choncho amene wapambana pa nkhondo+ adzavekedwa malaya akunja oyera.+ Ndipo sindidzafafaniza dzina lake m’buku la moyo,+ koma ndidzavomereza dzina lake pamaso pa Atate wanga,+ ndi pamaso pa angelo ake.+ 6 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu ukunena+ ku mipingo.’

7 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Filadefiya, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena woyerayo,+ amene ali woona,+ yemwe ali ndi kiyi wa Davide.+ Iye amene amati akatsegula palibe wina amene angatseke, ndipo akatseka palibe wina amene angatsegule. 8 ‘Ndikudziwa ntchito zako.+ Taona! Ndakutsegulira khomo+ pamaso pako, limene wina sangalitseke. Ndikudziwa kuti uli ndi mphamvu zochepa, ndiponso kuti unasunga mawu anga. Ndikudziwanso kuti wakhala wokhulupirika ku dzina langa.+ 9 Taona! Anthu ochokera m’sunagoge wa Satana, amene amanama+ kuti ndi Ayuda+ pamene si Ayuda, ndidzawachititsa kuti abwere kudzagwada ndi kuwerama+ pamapazi ako. Ndipo ndidzawachititsa kudziwa kuti ndimakukonda. 10 Popeza unasunga mawu onena za kupirira kwanga,+ inenso ndidzakusunga+ pa ola la kuyesedwa, limene likubwera padziko lonse lapansi kumene kuli anthu. Ndidzakusunga pa ola limene likubwera kudzayesa okhala padziko lapansi.+ 11 Ndikubwera mofulumira.+ Gwirabe mwamphamvu chimene uli nacho,+ kuti wina asakulande mphoto* yako.+

12 “‘Wopambana pa nkhondo, ndidzamuika kukhala mzati+ m’kachisi+ wa Mulungu wanga,+ ndipo sadzachokamonso. Ndidzamulemba dzina la Mulungu wanga, ndiponso dzina la mzinda wa Mulungu wanga, Yerusalemu watsopano,+ wotsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu wanga. Ndidzamulembanso dzina langa latsopano.+ 13 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu+ ukunena ku mipingo.’

14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+ 15 ‘Ndikudziwa ntchito zako, kuti si iwe wozizira kapena wotentha. Ndikanakonda ukanakhala wozizira kapena wotentha. 16 Choncho, chifukwa choti ndiwe wofunda, osati wotentha+ kapena wozizira,+ ndikulavula m’kamwa mwanga. 17 Iwe ukunena kuti: “Ndine wolemera,+ ndapeza chuma chambiri ndipo sindikusowa kanthu,” koma sukudziwa kuti ndiwe wovutika, womvetsa chisoni, wosauka, wakhungu,+ ndi wamaliseche. 18 Chotero, ndikukulangiza kuti ugule kwa ine golide+ woyengedwa ndi moto, kuti ukhale wolemera. Ugulenso malaya akunja oyera uvale, kuti maliseche ako asaonekere+ chifukwa ungachite manyazi. Ndiponso ugule mankhwala opaka m’maso+ ako kuti uone.

19 “‘Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula ndi kuwalanga.+ Choncho, khala wodzipereka ndipo ulape.+ 20 Taona! Ndaima pakhomo,+ ndipo ndikugogoda. Wina akamva mawu anga ndi kutsegula chitseko,+ ndidzalowa m’nyumba mwake ndipo iye ndi ine tidzadyera limodzi chakudya chamadzulo. 21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo. 22 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu+ ukunena ku mipingo.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena