Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 9
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 9:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:2
  • +Nu 24:17; Chv 22:16
  • +Chv 20:1
  • +Lu 8:31; Chv 9:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 143

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1989, ptsa. 17-18

    12/15/1988, ptsa. 12-13

Chivumbulutso 9:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 19:18; Yow 2:30
  • +Ge 19:28
  • +Yow 2:2, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 143-144

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 12-13

Chivumbulutso 9:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 10:4, 12
  • +De 8:15; Lu 11:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 143-144

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 12-13

Chivumbulutso 9:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 7:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 144-145, 147-148

Chivumbulutso 9:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:9; 18:7
  • +Chv 9:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 144-145, 147-148

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 12-13

Chivumbulutso 9:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 3:21; Chv 6:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 144-145

Chivumbulutso 9:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yow 2:4
  • +Yow 2:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 145-146, 153

Chivumbulutso 9:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 11:15; Aef 5:24
  • +Yow 1:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 145-146

Chivumbulutso 9:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 6:14; 1At 5:8; 2Ti 2:3
  • +Yow 2:5
  • +2Ak 10:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 145-146

Chivumbulutso 9:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 32

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 146-148

Chivumbulutso 9:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:1; 20:1
  • +Lu 4:34; Chv 19:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 143, 148

Chivumbulutso 9:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 148

Chivumbulutso 9:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:6
  • +Chv 11:15
  • +Chv 1:12
  • +Chv 8:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 148

Chivumbulutso 9:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 4:14
  • +Sl 102:20; 137:1; 142:7; Yes 42:7; 49:9
  • +Ge 2:14; Chv 16:12; 17:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 148-149

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 13

Chivumbulutso 9:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 149-151

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 13

Chivumbulutso 9:16

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “20,000 kuchulukitsa ndi 10,000,” imene ndi 200 miliyoni. Onani mawu a m’munsi pa Chv 5:11.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 149-153

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, tsa. 29

    12/15/1988, tsa. 13

Chivumbulutso 9:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mb 12:8; Miy 28:1
  • +Sl 11:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 149-153

Chivumbulutso 9:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 149-153

Chivumbulutso 9:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 8:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 32

    4/1/1989, tsa. 19

    12/15/1988, tsa. 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 153-154

Chivumbulutso 9:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 31:29; Yer 5:3
  • +De 32:17; Sl 106:37; 1Ak 10:20
  • +Sl 115:4; 135:15
  • +Yes 44:9; Yer 10:5; Da 5:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 32

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 154

Chivumbulutso 9:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 20:13
  • +Aga 5:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 32

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 154

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 9:1Chv 8:2
Chiv. 9:1Nu 24:17; Chv 22:16
Chiv. 9:1Chv 20:1
Chiv. 9:1Lu 8:31; Chv 9:11
Chiv. 9:2Eks 19:18; Yow 2:30
Chiv. 9:2Ge 19:28
Chiv. 9:2Yow 2:2, 10
Chiv. 9:3Eks 10:4, 12
Chiv. 9:3De 8:15; Lu 11:12
Chiv. 9:4Chv 7:3
Chiv. 9:5Chv 16:9; 18:7
Chiv. 9:5Chv 9:10
Chiv. 9:6Yob 3:21; Chv 6:16
Chiv. 9:7Yow 2:4
Chiv. 9:7Yow 2:6
Chiv. 9:81Ak 11:15; Aef 5:24
Chiv. 9:8Yow 1:6
Chiv. 9:9Aef 6:14; 1At 5:8; 2Ti 2:3
Chiv. 9:9Yow 2:5
Chiv. 9:92Ak 10:4
Chiv. 9:10Chv 9:5
Chiv. 9:11Chv 9:1; 20:1
Chiv. 9:11Lu 4:34; Chv 19:15
Chiv. 9:12Chv 8:13
Chiv. 9:13Chv 8:6
Chiv. 9:13Chv 11:15
Chiv. 9:13Chv 1:12
Chiv. 9:13Chv 8:3
Chiv. 9:14Aga 4:14
Chiv. 9:14Sl 102:20; 137:1; 142:7; Yes 42:7; 49:9
Chiv. 9:14Ge 2:14; Chv 16:12; 17:15
Chiv. 9:171Mb 12:8; Miy 28:1
Chiv. 9:17Sl 11:6
Chiv. 9:19Yer 8:17
Chiv. 9:20De 31:29; Yer 5:3
Chiv. 9:20De 32:17; Sl 106:37; 1Ak 10:20
Chiv. 9:20Sl 115:4; 135:15
Chiv. 9:20Yes 44:9; Yer 10:5; Da 5:23
Chiv. 9:21Eks 20:13
Chiv. 9:21Aga 5:20
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 9:1-21

Chivumbulutso

9 Kenako mngelo wachisanu analiza lipenga+ lake. Ndipo ndinaona nyenyezi+ imene inagwera kudziko lapansi kuchokera kumwamba. Nyenyeziyo inapatsidwa kiyi+ wa dzenje+ lolowera kuphompho. 2 Pamene inatsegula dzenje lolowera kuphompholo, utsi+ ngati wa m’ng’anjo yaikulu+ unatuluka m’dzenjemo, ndipo dzuwa ndi mpweya zinada+ ndi utsi wa m’dzenjewo. 3 Mu utsiwo, munatuluka dzombe+ n’kubwera padziko lapansi. Dzombelo linapatsidwa ulamuliro wofanana ndi umene zinkhanira+ za padziko lapansi zili nawo. 4 Ndipo linauzidwa kuti lisawononge zomera za padziko lapansi, kapena chilichonse chobiriwira, kapena mtengo uliwonse, koma livulaze anthu okhawo amene alibe chidindo cha Mulungu pamphumi pawo.+

5 Dzombelo silinaloledwe kupha anthuwo, koma linauzidwa kuti liwazunze+ miyezi isanu. Ndipo kuzunzika kwawo kunali kofanana ndi mmene munthu amazunzikira akalumidwa ndi chinkhanira.+ 6 M’masiku amenewo, anthuwo adzafunafuna imfa,+ koma sadzaipeza. Adzalakalaka kufa, koma imfa izidzawathawa.

7 Dzombelo linali kuoneka ngati mahatchi+ okonzekera nkhondo. Pamitu pawo panali zinthu zooneka ngati zisoti zachifumu zokhala ngati zagolide. Nkhope zawo zinali ngati nkhope za amuna,+ 8 koma tsitsi lawo linali ngati la akazi.+ Mano awo anali ngati a mikango.+ 9 Pachifuwa pawo panali zotetezera+ zokhala ngati zachitsulo. Ndipo phokoso la mapiko awo linali ngati phokoso la magaleta+ okokedwa ndi mahatchi ambiri omwe akuthamangira kunkhondo.+ 10 Dzombelo linali ndi michira ndi mbola ngati zinkhanira.+ M’michira yawoyo ndi mmene munali ulamuliro wawo wovulaza anthuwo kwa miyezi isanu. 11 Dzombelo lili ndi mfumu. Mfumuyo ndiye mngelo wa phompho.+ M’Chiheberi, dzina lake ndi Abadoni, koma m’Chigiriki ali ndi dzina lakuti Apoliyoni.+

12 Tsoka limodzilo linapita. Koma masoka ena awiri+ anali kubwera pambuyo pa zimenezi.

13 Kenako mngelo wa 6+ analiza lipenga+ lake. Ndipo ndinamva mawu amodzi+ kuchokera panyanga za paguwa lansembe lagolide+ lokhala pamaso pa Mulungu. 14 Mawuwo anauza mngelo wa 6 amene anali ndi lipengayo kuti: “Masula angelo anayi+ omangidwa+ amene ali kumtsinje waukulu wa Firate.”+ 15 Angelo anayiwo anamasulidwa. Iwo anali okonzekera kuti pa ola, tsiku, mwezi, ndi chaka chimenecho, aphe gawo limodzi mwa magawo atatu a anthu.

16 Ndipo chiwerengero cha makamu a asilikali okwera pamahatchi, chinali miyanda iwiri kuchulukitsa ndi miyanda.* Chimenechi ndicho chiwerengero chawo chimene ndinamva. 17 Mahatchi ndi okwerapowo ndinawaona motere m’masomphenyawo: Anavala zoteteza pachifuwa zofiira ngati moto, zobiriwira ngati mwala wa huwakinto, ndi zachikasu ngati sulufule. Mitu ya mahatchiwo inali ngati mitu ya mikango,+ ndipo m’kamwa mwawo munali kutuluka moto, utsi, ndi sulufule.+ 18 M’kamwa mwawomo munalinso kutuluka miliri itatu iyi: Moto, utsi, ndi sulufule, ndipo inapha gawo limodzi mwa magawo atatu a anthu. 19 Ulamuliro wa mahatchiwo unali m’kamwa mwawo ndi m’michira yawo, pakuti michira yawo inali ngati njoka,+ ndipo inali ndi mitu. Zinthu zimenezi anali kuwononga nazo anthu.

20 Koma anthu ena onse amene sanaphedwe ndi miliri imeneyi, sanalape ntchito za manja awo.+ Sanalape kulambira ziwanda+ ndi mafano agolide, asiliva,+ amkuwa, amwala, ndi amtengo, mafano amene sangathe kuona, kumva, kapena kuyenda.+ 21 Iwo sanalape ntchito zawo zopha anthu,+ zamizimu,+ dama lawo, ngakhalenso umbava wawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena