Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 6
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Mwanawankhosa anamatula zidindo 6 zoyambirira (1-17)

        • Wogonjetsa adani anakwera pahatchi yoyera (1, 2)

        • Amene anakwera pahatchi yofiira ngati moto analoledwa kuchotsa mtendere (3, 4)

        • Amene anakwera pahatchi yakuda anabweretsa njala (5, 6)

        • Amene anakwera pahatchi yotuwa dzina lake ndi Imfa (7, 8)

        • Pansi pa guwa lansembe panali anthu amene anaphedwa (9-11)

        • Chivomerezi chachikulu (12-17)

Chivumbulutso 6:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:6
  • +Chv 5:5
  • +Chv 4:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 89-90

Chivumbulutso 6:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 19:11
  • +Chv 14:14
  • +Sl 45:4; 110:1, 2; Chv 12:7; 17:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    11/2019, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 4, 6, 8

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2014, ptsa. 5, 7

    2/1/2014, tsa. 6

    9/15/2010, tsa. 29

    4/15/2009, tsa. 30

    1/15/2005, tsa. 17

    6/1/2001, ptsa. 17-22

    10/15/1988, ptsa. 10-11, 15-16

    1/15/1986, ptsa. 3, 6

    1/1/1986, ptsa. 3, 4-6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 90-93

    Galamukani!,

    5/8/1988, ptsa. 14-16

Chivumbulutso 6:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 93

Chivumbulutso 6:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 24:7; Lu 21:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2014, tsa. 6

    9/1/2005, ptsa. 19-20

    9/15/1998, tsa. 7

    3/1/1993, ptsa. 4-5

    1/15/1986, ptsa. 3-4

    1/1/1986, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 93-95

    Mawu a Mulungu, ptsa. 137-139

    Galamukani!,

    5/8/1988, ptsa. 3, 5-6, 7-9

    3/8/1988, ptsa. 15-16

    Mtendere Weniweni, ptsa. 10, 11-12

Chivumbulutso 6:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:5
  • +Chv 4:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 5, 7

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2014, tsa. 7

    1/15/1986, ptsa. 3-5

    1/1/1986, ptsa. 6-7

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 95

    Mawu a Mulungu, ptsa. 139-141

    Galamukani!,

    5/8/1988, ptsa. 3, 9-10

Chivumbulutso 6:6

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “kwati imodzi.” Onani Zakumapeto B14.

  • *

    Imeneyi ndi ndalama ya siliva ya Aroma ndipo inali malipiro antchito imene munthu wagwira tsiku limodzi. Onani Zakumapeto B14.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 20:2
  • +Mko 13:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 5, 7

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 96

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/1998, tsa. 7

    8/1/1995, tsa. 4

    1/15/1986, ptsa. 3-5

    Mawu a Mulungu, ptsa. 139-141

Chivumbulutso 6:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 96

Chivumbulutso 6:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Amenewa ndi manda a anthu onse. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 21:11
  • +Yer 15:2, 3; Eze 14:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 3 2017, tsatsa. 5, 7

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2014, tsa. 7

    5/1/2005, tsa. 17

    5/15/1993, tsa. 31

    10/15/1988, ptsa. 11-12

    1/15/1986, ptsa. 3, 5

    1/1/1986, tsa. 7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 96-98

    Galamukani!,

    10/8/1994, tsa. 30

    5/8/1988, ptsa. 3, 10-11

    Mawu a Mulungu, ptsa. 142-146

    Mtendere Weniweni, ptsa. 14-15

Chivumbulutso 6:9

Mawu a M'munsi

  • *

    Nʼkutheka kuti apa akunena za magazi amene anathiridwa paguwa lansembe. Magazi amenewa akuimira moyo.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Le 4:7; Chv 8:3
  • +Le 17:11
  • +Mt 24:9, 14; Yoh 18:37; Chv 17:6; 20:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, ptsa. 28-29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 100, 289

Chivumbulutso 6:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 5:20
  • +De 32:43; Lu 18:7; Chv 19:1, 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 101-102, 245, 289

Chivumbulutso 6:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:5
  • +Mt 24:9; Mac 9:1; 2Ak 1:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, ptsa. 29-30

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 102-104, 289

Chivumbulutso 6:12

Mawu a M'munsi

  • *

    Nʼkutheka kuti akunena ubweya wa mbuzi.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yow 2:31; Mt 24:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 104-110

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, tsa. 17

Chivumbulutso 6:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 109-110

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, tsa. 17

Chivumbulutso 6:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 34:4
  • +Chv 16:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    4/2017, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 110-112

Chivumbulutso 6:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 2:10, 19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 16

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 112

Chivumbulutso 6:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ho 10:8; Lu 23:30
  • +Chv 4:2, 3
  • +Chv 5:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 112

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1997, tsa. 20

Chivumbulutso 6:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zef 1:14, 18; Aro 2:5
  • +Yow 2:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2014, tsa. 31

    12/15/1988, ptsa. 11-12

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 112-113, 128-129

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 6:1Chv 5:6
Chiv. 6:1Chv 5:5
Chiv. 6:1Chv 4:7
Chiv. 6:2Chv 19:11
Chiv. 6:2Chv 14:14
Chiv. 6:2Sl 45:4; 110:1, 2; Chv 12:7; 17:14
Chiv. 6:3Chv 4:7
Chiv. 6:4Mt 24:7; Lu 21:10
Chiv. 6:5Chv 5:5
Chiv. 6:5Chv 4:7
Chiv. 6:6Mt 20:2
Chiv. 6:6Mko 13:8
Chiv. 6:7Chv 4:7
Chiv. 6:8Lu 21:11
Chiv. 6:8Yer 15:2, 3; Eze 14:21
Chiv. 6:9Le 4:7; Chv 8:3
Chiv. 6:9Le 17:11
Chiv. 6:9Mt 24:9, 14; Yoh 18:37; Chv 17:6; 20:4
Chiv. 6:101Yo 5:20
Chiv. 6:10De 32:43; Lu 18:7; Chv 19:1, 2
Chiv. 6:11Chv 3:5
Chiv. 6:11Mt 24:9; Mac 9:1; 2Ak 1:8
Chiv. 6:12Yow 2:31; Mt 24:29
Chiv. 6:14Yes 34:4
Chiv. 6:14Chv 16:20
Chiv. 6:15Yes 2:10, 19
Chiv. 6:16Ho 10:8; Lu 23:30
Chiv. 6:16Chv 4:2, 3
Chiv. 6:16Chv 5:6
Chiv. 6:17Zef 1:14, 18; Aro 2:5
Chiv. 6:17Yow 2:11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 6:1-17

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

6 Ndinaona Mwanawankhosa+ akumatula chidindo chimodzi mwa zidindo 7 zija,+ ndipo ndinamva mngelo mmodzi mwa angelo 4 aja+ akulankhula ndi mawu omveka ngati kugunda kwa bingu kuti: “Bwera!” 2 Nditayangʼana, ndinaona hatchi yoyera+ ndipo amene anakwera pahatchiyi ananyamula uta. Iye anapatsidwa chisoti chachifumu+ nʼkupita kukagonjetsa adani ake ndipo anapambana pankhondo yolimbana nawo.+

3 Atamatula chidindo chachiwiri, ndinamva mngelo wachiwiri+ akunena kuti: “Bwera!” 4 Panatuluka hatchi ina yofiira ngati moto. Amene anakwera pahatchi imeneyi analoledwa kuchotsa mtendere padziko lapansi, kuti anthu aphane ndipo anapatsidwa lupanga lalikulu.+

5 Atamatula chidindo chachitatu,+ ndinamva mngelo wachitatu+ akunena kuti: “Bwera!” Ndipo nditayangʼana, ndinaona hatchi yakuda. Amene anakwera pahatchiyo anali ndi sikelo mʼdzanja lake. 6 Kenako ndinamva ngati wina akulankhula kuchokera pakati pa angelo 4 aja kuti: “Kilogalamu imodzi* ya tirigu, mtengo wake ukhala dinari* imodzi,+ ndipo makilogalamu atatu a balere, mtengo wake ukhala dinari imodzi. Koma musawononge mafuta a maolivi ndi vinyo.”+

7 Atamatula chidindo cha 4, ndinamva mawu a mngelo wa 4+ akunena kuti: “Bwera!” 8 Nditayangʼana, ndinaona hatchi yotuwa. Amene anakwera pahatchiyi dzina lake anali Imfa. Ndipo Manda* ankamutsatira pafupi kwambiri. Iwo anapatsidwa ulamuliro pa gawo limodzi la magawo 4 adziko lapansi, kuti aphe anthu ndi lupanga lalitali, njala,+ mliri woopsa komanso zilombo zapadziko lapansi.+

9 Atamatula chidindo cha 5, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo*+ ya anthu amene anaphedwa chifukwa cha mawu a Mulungu ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni.+ 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera mpaka liti, inu Ambuye Wamkulu Koposa, Mulungu woyera ndi woona,+ osaweruza ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi athu?”+ 11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pangʼono, mpaka chiwerengero cha akapolo anzawo chitakwanira, inde chiwerengero cha abale awo amene anali atatsala pangʼono kuphedwa ngati mmenenso iwowo anaphedwera.+

12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomerezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli choluka ndi ubweya* ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+ 13 Nyenyezi zakumwamba zinagwera padziko lapansi ngati mmene mtengo wa mkuyu umene ukugwedezeka ndi mphepo yamphamvu umagwetsera nkhuyu zake zosapsa. 14 Ndipo kumwamba kunachoka ngati mpukutu umene akuupinda,+ ndipo phiri lililonse ndi chilumba chilichonse zinachotsedwa pamalo ake.+ 15 Kenako mafumu apadziko lapansi, nduna, akuluakulu a asilikali, olemera, amphamvu, kapolo aliyense ndi munthu aliyense amene ndi mfulu, anabisala mʼmapanga ndi mʼmatanthwe amʼmapiri.+ 16 Iwo ankauza mapiri ndi matanthwe kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Mulungu amene wakhala pampando wachifumu+ ndiponso kuti mkwiyo wa Mwanawankhosa usatigwere,+ 17 chifukwa tsiku lalikulu la mkwiyo wawo lafika,+ ndipo ndi ndani amene angaimirire pamaso pawo?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena