Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nyimbo ya Solomo 8
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Nyimbo ya Solomo 8:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 1:6
  • +Aga 4:26
  • +Sl 2:12; Nym 1:2

Nyimbo ya Solomo 8:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 3:4
  • +Miy 9:2; Nym 5:1

Nyimbo ya Solomo 8:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 2:6

Nyimbo ya Solomo 8:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 2:7; 3:5

Nyimbo ya Solomo 8:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 6:13; 7:10
  • +Sl 45:10
  • +Nym 7:11
  • +Ge 3:16

Nyimbo ya Solomo 8:6

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 5.

  • *

    Awa ndi malo okhawo m’buku la Nyimbo ya Solomo pamene pakupezeka dzina la Mulungu. Panopa, lalembedwa mwachidule kuti “Ya.” Onani mawu a m’munsi pa Eks 15:2 ndi Zakumapeto 1.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Hag 2:23
  • +Yoh 15:13; Aro 16:4; Aef 5:25; Chv 12:11
  • +Eks 20:5; Yos 24:19
  • +Sl 89:8; 118:17; Yes 12:2; 1Yo 4:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2023, tsa. 20

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2015, tsa. 29

    5/15/2012, tsa. 4

    11/15/2006, tsa. 20

    11/15/1987, tsa. 25

Nyimbo ya Solomo 8:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 13:8, 13
  • +Aro 8:39

Nyimbo ya Solomo 8:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 1:6

Nyimbo ya Solomo 8:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 7:1; Aga 5:23; 1Pe 3:2
  • +Miy 7:11; Ho 2:7; 1Ak 7:9

Nyimbo ya Solomo 8:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 7:34; Akl 3:5; 1Pe 2:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Galamukani!,

    3/8/1992, tsa. 10

Nyimbo ya Solomo 8:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mla 2:4; Nym 7:12
  • +Lu 20:9

Nyimbo ya Solomo 8:13

Mawu a M'munsi

  • *

    Mwina akutanthauzanso, “anzako.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 1:6; 6:11
  • +Nym 2:14

Nyimbo ya Solomo 8:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 2:17

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Nyimbo 8:1Nym 1:6
Nyimbo 8:1Aga 4:26
Nyimbo 8:1Sl 2:12; Nym 1:2
Nyimbo 8:2Nym 3:4
Nyimbo 8:2Miy 9:2; Nym 5:1
Nyimbo 8:3Nym 2:6
Nyimbo 8:4Nym 2:7; 3:5
Nyimbo 8:5Nym 6:13; 7:10
Nyimbo 8:5Sl 45:10
Nyimbo 8:5Nym 7:11
Nyimbo 8:5Ge 3:16
Nyimbo 8:6Hag 2:23
Nyimbo 8:6Yoh 15:13; Aro 16:4; Aef 5:25; Chv 12:11
Nyimbo 8:6Eks 20:5; Yos 24:19
Nyimbo 8:6Sl 89:8; 118:17; Yes 12:2; 1Yo 4:8
Nyimbo 8:71Ak 13:8, 13
Nyimbo 8:7Aro 8:39
Nyimbo 8:8Nym 1:6
Nyimbo 8:92Ak 7:1; Aga 5:23; 1Pe 3:2
Nyimbo 8:9Miy 7:11; Ho 2:7; 1Ak 7:9
Nyimbo 8:101Ak 7:34; Akl 3:5; 1Pe 2:12
Nyimbo 8:11Mla 2:4; Nym 7:12
Nyimbo 8:11Lu 20:9
Nyimbo 8:13Nym 1:6; 6:11
Nyimbo 8:13Nym 2:14
Nyimbo 8:14Nym 2:17
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Nyimbo ya Solomo 8:1-14

Nyimbo ya Solomo

8 “Ndikulakalaka ukanakhala ngati mlongo wanga,+ amene anayamwa mabere a mayi anga.+ Ndikanakupeza panja ndikanakupsompsona,+ ndipo anthu sakanandinyoza n’komwe. 2 Bwenzi nditakutsogolera ndipo ndikanakulowetsa m’nyumba mwa mayi anga,+ amene ankandiphunzitsa. Ndikanakupatsa vinyo wothira zonunkhiritsa,+ ndi madzi a makangaza ongofinya kumene. 3 Dzanja lake lamanzere likanakhala pansi pa mutu wanga, ndipo dzanja lake lamanja likanandikumbatira.+

4 “Ndakulumbiritsani inu ana aakazi a ku Yerusalemu, kuti musayese kudzutsa chikondi mwa ine mpaka pamene chikondicho chifunire.”+

5 “Kodi mkazi+ amene akuchokera kuchipululuyu ndani,+ atakoloweka dzanja lake m’khosi mwa wachikondi wake?”+

“Ine ndinakudzutsa pansi pa mtengo wa maapozi. Pamenepo m’pamene mayi ako anamva zowawa pokubereka. Mayi amene anali kukubereka anamva zowawa ali pamenepo.+

6 “Undiike pamtima pako ngati chidindo,+ ndiponso undiike ngati chidindo padzanja lako, chifukwa chikondi n’champhamvu ngati imfa.+ Mofanana ndi Manda,* chikondi sichigonja ndipo chimafuna kudzipereka ndi mtima wonse.+ Kuyaka kwake kuli ngati kuyaka kwa moto. Chikondicho ndi lawi la Ya.*+ 7 Madzi ambiri sangathe kuzimitsa chikondi,+ ndipo mitsinje singachikokolole.+ Munthu atapereka zinthu zonse zamtengo wapatali za m’nyumba mwake posinthanitsa ndi chikondi, anthu anganyoze zinthuzo.”

8 “Tili ndi mlongo wathu wamng’ono+ amene alibe mabere. Kodi tidzamuchitire chiyani tsiku limene adzafunsiridwe ukwati?”

9 “Akadzakhala khoma,+ tidzam’mangira kansanja kasiliva pamwamba pake, koma akadzakhala chitseko,+ tidzam’khomerera ndi thabwa la mkungudza.”

10 “Ine ndine khoma, ndipo mabere anga ali ngati nsanja.+ Choncho m’maso mwake ndakhala ngati mkazi amene wapeza mtendere.

11 “Solomo anali ndi munda wa mpesa+ ku Baala-hamoni. Munda wa mpesawo anaupereka kwa anthu oti aziusamalira.+ Munthu aliyense anali kubweretsa ndalama zasiliva zokwana 1,000 zolipirira zipatso za mundawo.

12 “Munda wanga wa mpesa ndingathe kuchita nawo chilichonse. Ndalama 1,000 zasilivazo ndi zanu inu a Solomo, ndipo ndalama zasiliva 200 ndi za anthu amene amatenga zipatso za munda wanu wa mpesa.”

13 “Iwe amene ukukhala m’minda,+ anzanga* akufuna amve mawu ako. Inenso ndikufuna ndimve mawu ako.”+

14 “Thamanga wachikondi wanga. Ukhale ngati insa kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri pamene pamamera maluwa onunkhira.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena