Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nyimbo ya Solomo 2
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Nyimbo ya Solomo 2:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 35:1
  • +1Mb 27:29
  • +Nym 2:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2015, ptsa. 31-32

    11/15/1987, tsa. 24

Nyimbo ya Solomo 2:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 1:15; Afi 2:15; 1Pe 2:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2015, ptsa. 31-32

    11/15/1987, tsa. 24

Nyimbo ya Solomo 2:3

Mawu a M'munsi

  • *

    Ena amati “chonzuna.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 8:5
  • +Sl 45:2; Nym 5:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/1987, tsa. 24

Nyimbo ya Solomo 2:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 25:6
  • +Ge 29:18, 20
  • +Nym 6:4

Nyimbo ya Solomo 2:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Sa 30:12; 2Sa 6:19
  • +1Sa 18:20; Nym 5:8

Nyimbo ya Solomo 2:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 8:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2006, tsa. 18

Nyimbo ya Solomo 2:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 6:13
  • +2Sa 2:18; 1Mb 12:8; Nym 3:5
  • +Miy 5:19
  • +Nym 8:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2015, tsa. 31

    11/15/2006, ptsa. 18-19

    11/15/1987, ptsa. 24-25

Nyimbo ya Solomo 2:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 5:2; Yoh 10:27; Chv 3:20
  • +Chv 22:20

Nyimbo ya Solomo 2:9

Mawu a M'munsi

  • *

    Ena amati “chipupa,” kapena “chikupa.”

  • *

    Pawindo limeneli panali potchingidwa ndi timatabwa tolukanalukana.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 2:17; 8:14
  • +Owe 5:28

Nyimbo ya Solomo 2:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 4:7
  • +Sl 45:10; Yoh 14:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2015, tsa. 32

    Galamukani!,

    4/8/1994, ptsa. 24-25

Nyimbo ya Solomo 2:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zek 10:1

Nyimbo ya Solomo 2:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 6:11; Yes 55:10
  • +Yes 18:5; Yoh 15:2
  • +Yer 8:7

Nyimbo ya Solomo 2:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mik 4:4
  • +Yes 28:4; Nah 3:12
  • +Nym 1:15

Nyimbo ya Solomo 2:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 5:2; Yer 48:28; Mt 10:16
  • +Sl 45:11
  • +Nym 1:5; 6:10

Nyimbo ya Solomo 2:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Owe 15:4; Mlr 5:18
  • +Nym 7:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Galamukani!,

    4/8/1994, ptsa. 24-25

Nyimbo ya Solomo 2:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 6:3; 7:10
  • +Nym 1:7
  • +Nym 2:1

Nyimbo ya Solomo 2:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Sa 2:18; Nym 2:9; 8:14

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Nyimbo 2:1Yes 35:1
Nyimbo 2:11Mb 27:29
Nyimbo 2:1Nym 2:16
Nyimbo 2:2Nym 1:15; Afi 2:15; 1Pe 2:12
Nyimbo 2:3Nym 8:5
Nyimbo 2:3Sl 45:2; Nym 5:9
Nyimbo 2:4Yes 25:6
Nyimbo 2:4Ge 29:18, 20
Nyimbo 2:4Nym 6:4
Nyimbo 2:51Sa 30:12; 2Sa 6:19
Nyimbo 2:51Sa 18:20; Nym 5:8
Nyimbo 2:6Nym 8:3
Nyimbo 2:7De 6:13
Nyimbo 2:72Sa 2:18; 1Mb 12:8; Nym 3:5
Nyimbo 2:7Miy 5:19
Nyimbo 2:7Nym 8:4
Nyimbo 2:8Nym 5:2; Yoh 10:27; Chv 3:20
Nyimbo 2:8Chv 22:20
Nyimbo 2:9Nym 2:17; 8:14
Nyimbo 2:9Owe 5:28
Nyimbo 2:10Nym 4:7
Nyimbo 2:10Sl 45:10; Yoh 14:3
Nyimbo 2:11Zek 10:1
Nyimbo 2:12Nym 6:11; Yes 55:10
Nyimbo 2:12Yes 18:5; Yoh 15:2
Nyimbo 2:12Yer 8:7
Nyimbo 2:13Mik 4:4
Nyimbo 2:13Yes 28:4; Nah 3:12
Nyimbo 2:13Nym 1:15
Nyimbo 2:14Nym 5:2; Yer 48:28; Mt 10:16
Nyimbo 2:14Sl 45:11
Nyimbo 2:14Nym 1:5; 6:10
Nyimbo 2:15Owe 15:4; Mlr 5:18
Nyimbo 2:15Nym 7:12
Nyimbo 2:16Nym 6:3; 7:10
Nyimbo 2:16Nym 1:7
Nyimbo 2:16Nym 2:1
Nyimbo 2:172Sa 2:18; Nym 2:9; 8:14
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Nyimbo ya Solomo 2:1-17

Nyimbo ya Solomo

2 “Ine ndine duwa lonyozeka+ la m’chigwa cha m’mphepete mwa nyanja.+ Inetu ndine duwa la m’chigwa.”+

2 “Monga duwa pakati pa zitsamba zaminga, ndi mmene alili wokondedwa wanga pakati pa ana aakazi.”+

3 “Monga mtengo wa maapozi+ pakati pa mitengo ya m’nkhalango, ndi mmene alili wachikondi wanga pakati pa ana aamuna.+ Ineyo ndinali kulakalaka mthunzi wa wokondedwa wanga ndipo ndinakhala pansi, pamthunzi wakewo. Chipatso chake chinali chotsekemera* m’kamwa mwanga. 4 Iye anandipititsa kunyumba ya phwando la vinyo,+ ndipo chikondi+ chake kwa ine chinali ngati mbendera+ yozikidwa pambali panga. 5 Anthu inu ndipatseni mphesa zouma zoumba pamodzi kuti zinditsitsimule.+ Ndipatseni maapozi kuti ndisafe chifukwa chikondi chikundidwalitsa.+ 6 Dzanja lake lamanzere lili pansi pa mutu wanga, ndipo dzanja lake lamanja landikumbatira.+ 7 Ndakulumbiritsani inu+ ana aakazi a ku Yerusalemu, pali mbawala zazikazi+ ndiponso pali mphoyo+ zakutchire, kuti musayese kudzutsa chikondi mwa ine mpaka pamene chikondicho chifunire.+

8 “Ndikumva wachikondi wanga+ akubwera.+ Akukwera mapiri ndipo akudumphadumpha pazitunda. 9 Wachikondi wanga akufanana ndi mbawala+ kapena mphoyo yaing’ono. Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma* la nyumba yathu. Akuyang’ana m’mawindo,* akusuzumira pa zotchingira m’mawindo.+ 10 Wachikondi wanga wandiuza kuti, ‘Nyamuka wokondedwa wanga wokongolawe,+ tiye tizipita.+ 11 Taona! Nyengo yamvula yatha,+ mvula yaleka, yapita kwawo. 12 Maluwa ayamba kuoneka m’dziko,+ nthawi yodulira mpesa+ yakwana, ndipo m’dziko lathu mukumveka kulira kwa njiwa.+ 13 Pamtengo wa mkuyu,+ nkhuyu zoyambirira zapsa.+ Mpesa wachita maluwa ndipo ukununkhira. Nyamuka, bwera kuno wokondedwa wanga+ wokongola, tiye tizipita. 14 Iwe njiwa yanga,+ tuluka m’malo obisika a pathanthwe. Tuluka pamalo osaoneka m’mphepete mwa njira yotsetsereka. Ndikufuna ndione thupi lako lokongola.+ Ndikufuna kumva mawu ako, chifukwa mawu ako ndi okoma ndipo iweyo ndiwe wokongola.’”+

15 “Anthu inu mutigwirire nkhandwe+ zing’onozing’ono zimene zikuwononga minda ya mpesa, chifukwa minda yathu ya mpesa yachita maluwa.”+

16 “Wachikondi wanga ndi wanga, ndipo ine ndine wake.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa am’tchire.+ 17 Mpaka nthawi ya kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka, tembenuka wachikondi wanga. Ukhale ngati mbawala+ kapena ngati mphoyo yaing’ono pamapiri amene akutilekanitsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena