Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 28
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Machitidwe 28:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 27:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 209-210

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2004, ptsa. 30-31

Machitidwe 28:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 19:22; Mac 27:3
  • +2Ak 11:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 209-210

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2002, tsa. 19

    5/1/1999, tsa. 30

Machitidwe 28:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 210

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 25

Machitidwe 28:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 210

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/2015, tsa. 9

    5/1/1999, ptsa. 30-31

Machitidwe 28:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 10:19

Machitidwe 28:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 14:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 210

Machitidwe 28:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 210

Machitidwe 28:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Mawu ake enieni, “kutentha thupi.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mko 7:32; Mac 19:11; 1Ak 12:9
  • +Lu 4:39

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 210

Machitidwe 28:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 10:8

Machitidwe 28:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/1991, tsa. 23

Machitidwe 28:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 27:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 211

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2009, tsa. 9

    6/15/1990, tsa. 25

    5/15/1990, tsa. 26

Machitidwe 28:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 211

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2007, tsa. 30

Machitidwe 28:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 211

Machitidwe 28:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 211-212

Machitidwe 28:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 1:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 212-213

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    11/2020, ptsa. 16-17

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2010, tsa. 11

    10/15/2006, ptsa. 14, 16-17

    12/15/2004, ptsa. 16-17

Machitidwe 28:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 213

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2013, tsa. 14

Machitidwe 28:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:12; 25:8
  • +Mac 21:33

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 213-214

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2001, tsa. 24

Machitidwe 28:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:10
  • +Mac 26:32
  • +Mac 23:9, 29; 25:25; 26:31

Machitidwe 28:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 25:11; 26:32

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 213-214

Machitidwe 28:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:6; 26:6; Tit 2:13
  • +Aef 6:20; 2Ti 1:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 214

Machitidwe 28:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 214

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2001, tsa. 24

Machitidwe 28:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:14
  • +Lu 2:34; Yoh 15:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/1994, tsa. 5

    7/1/1993, ptsa. 5-6, 15

Machitidwe 28:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 17:2; 26:22
  • +Ge 3:15; 22:18; 49:10; De 18:18; 32:43; Yoh 5:46
  • +Yes 9:6; 11:10; 52:15; Yer 23:5; Mik 5:2; Zek 13:7; Mki 3:1; Lu 24:44

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 215

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, ptsa. 12-13

Machitidwe 28:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 17:4
  • +Mac 14:4; 2At 3:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2003, ptsa. 22-23

Machitidwe 28:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 215

    Yesaya 1, tsa. 100

Machitidwe 28:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 6:9; Yer 5:31; Eze 12:2; Aro 11:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Yesaya 1, tsa. 100

Machitidwe 28:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 6:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 215

    Yesaya 1, tsa. 100

Machitidwe 28:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 3:6; Mac 13:46; 22:21; Aro 11:11
  • +Sl 67:2; 98:3; Yes 11:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 215

Machitidwe 28:29

Mawu a M'munsi

  • *

    Za mawu amene palibe, onani mawu a m’munsi pa Mt 17:21.

Machitidwe 28:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 28:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 215-217

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2013, ptsa. 14-15

    1/15/2007, tsa. 32

    12/15/2001, tsa. 24

    6/15/1990, tsa. 25

Machitidwe 28:31

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 26:26; Aef 6:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 215-217

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2013, ptsa. 14-15

    1/15/2007, tsa. 32

    5/15/2006, tsa. 14

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 28:1Mac 27:26
Mac. 28:2Miy 19:22; Mac 27:3
Mac. 28:22Ak 11:27
Mac. 28:5Lu 10:19
Mac. 28:6Mac 14:11
Mac. 28:8Mko 7:32; Mac 19:11; 1Ak 12:9
Mac. 28:8Lu 4:39
Mac. 28:9Mt 10:8
Mac. 28:11Mac 27:6
Mac. 28:152Ak 1:4
Mac. 28:16Mac 24:23
Mac. 28:17Mac 24:12; 25:8
Mac. 28:17Mac 21:33
Mac. 28:18Mac 24:10
Mac. 28:18Mac 26:32
Mac. 28:18Mac 23:9, 29; 25:25; 26:31
Mac. 28:19Mac 25:11; 26:32
Mac. 28:20Mac 23:6; 26:6; Tit 2:13
Mac. 28:20Aef 6:20; 2Ti 1:16
Mac. 28:22Mac 24:14
Mac. 28:22Lu 2:34; Yoh 15:19
Mac. 28:23Mac 17:2; 26:22
Mac. 28:23Ge 3:15; 22:18; 49:10; De 18:18; 32:43; Yoh 5:46
Mac. 28:23Yes 9:6; 11:10; 52:15; Yer 23:5; Mik 5:2; Zek 13:7; Mki 3:1; Lu 24:44
Mac. 28:24Mac 17:4
Mac. 28:24Mac 14:4; 2At 3:2
Mac. 28:26Yes 6:9; Yer 5:31; Eze 12:2; Aro 11:8
Mac. 28:27Yes 6:10
Mac. 28:28Lu 3:6; Mac 13:46; 22:21; Aro 11:11
Mac. 28:28Sl 67:2; 98:3; Yes 11:10
Mac. 28:30Mac 28:16
Mac. 28:31Mac 26:26; Aef 6:19
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 28:1-31

Machitidwe

28 Titapulumuka choncho, tinamva kuti chilumbacho chimatchedwa Melita.+ 2 Ndipo anthu olankhula chinenero chachilendo kumeneko anatisonyeza kukoma mtima kwapadera.+ Iwo anasonkha moto ndi kutilandira bwino tonse chifukwa kunali kugwa mvula ndiponso kuzizira.+ 3 Koma pamene Paulo anatola kamtolo ka nkhuni ndi kukaika pamoto, panatuluka njoka ya mphiri chifukwa cha kutentha ndipo inaluma ndi kukanirira kudzanja la Paulo. 4 Anthu achinenero chachilendowo ataona njoka yapoizoni ikulendewera kudzanja lake, anayamba kuuzana kuti: “Ndithu munthu uyu ndi wopha anthu, chifukwa ngakhale wapulumuka panyanja, chilungamo sichinamulole kuti akhalebe ndi moyo.” 5 Koma iye anakutumulira njoka yapoizoniyo pamoto, ndipo sinamuvulaze.+ 6 Iwo anali kuyembekezera kuti atupa kapena agwa mwadzidzidzi n’kufa. Koma atayembekezera nthawi yaitali n’kuona kuti palibe choopsa chimene chikumuchitikira, anasintha maganizo awo ndi kuyamba kumunena kuti ndi mulungu.+

7 Tsopano pafupi ndi malo amenewa, panali minda ya munthu woyang’anira chilumbacho, dzina lake Papuliyo. Iyeyu anatilandira ndi kutichereza bwino kwambiri masiku atatu. 8 Koma kunapezeka kuti bambo ake a Papuliyo anali chigonere akuvutika ndi malungo* komanso kamwazi. Choncho Paulo analowa mmene bambowo anali ndi kupemphera, ndipo anasanjika manja ake+ pa iwo ndi kuwachiritsa.+ 9 Izi zitachitika, anthu ena onse pachilumbacho amene anali kudwala, nawonso anabwera kwa iye ndipo anawachiritsa.+ 10 Iwo anatilemekeza mwa kutipatsa mphatso zambiri, komanso pamene tinali kunyamuka ulendo wathu, anatipatsa zinthu zochuluka zimene tinali kuzisowa.

11 Patapita miyezi itatu, tinanyamuka pangalawa ya ku Alekizandiriya.+ Ngalawa imeneyi inaima pachilumbapo kuyembekezera kuti nyengo yachisanu ithe, ndipo inali ndi chizindikiro cha “Ana Amapasa a Zeu.” 12 Kenako tinafika padoko ku Surakusa ndipo tinakhala pamenepo masiku atatu. 13 Pochoka kumeneko, tinazungulira ndi kukafika ku Regio. Patapita tsiku limodzi, kunayamba kuwomba mphepo ya kum’mwera, ndipo pa tsiku lachiwiri tinafika ku Potiyolo. 14 Kumeneko tinapeza abale ndipo anatichonderera kuti tikhale nawo masiku 7. Kenako tinapitiriza ulendo kulowera ku Roma. 15 Abale akumeneko atamva za ife, anabwera kudzatichingamira ku Msika wa Apiyo ndi ku Nyumba Zitatu za Alendo. Paulo atawaona, anayamika Mulungu, ndipo analimba mtima.+ 16 Pamapeto pake, titalowa mu Roma, Paulo analoledwa+ kumakhala yekha ndi msilikali womulondera.

17 Patapita masiku atatu, Paulo anasonkhanitsa akuluakulu a Ayuda. Atasonkhana pamodzi, anawauza kuti: “Amuna inu, abale anga, ngakhale kuti sindinachite kanthu kotsutsana ndi anthu kapena mwambo wa makolo athu,+ ndinagwidwa mu Yerusalemu ndi kuperekedwa m’manja mwa Aroma monga mkaidi.+ 18 Ndipo iwowa atafufuza,+ anali ofunitsitsa kundimasula,+ pakuti sanapeze chifukwa mwa ine choyenera chilango cha imfa.+ 19 Koma Ayuda atapitiriza kutsutsa zimenezo, ndinakakamizika kupempha+ kudzaonekera kwa Kaisara, komatu sikuti ndinali ndi kanthu koti ndidzaneneze mtundu wanga ayi. 20 Pa chifukwa chimenechi, ndinapempha kuti ndikuoneni ndi kulankhula nanu, pakuti ndamangidwa ndi unyolo uwu+ chifukwa cha chiyembekezo+ cha Isiraeli.” 21 Iwo anamuyankha kuti: “Ife sitinalandire makalata alionse ochokera ku Yudeya onena za iwe. Palibenso aliyense mwa abale amene afika kuno, amene wanena kapena kukambapo choipa chilichonse chokhudza iwe. 22 Komabe tikufuna kumva maganizo ako, chifukwa kunena zoona, ife tonse timadziwa kuti gulu lampatuko limeneli+ amalinenera zoipa kwina kulikonse.”+

23 Pamenepo iwo anapangana naye tsiku, ndipo anabwera mwaunyinji kumene iye anali kukhala. Chotero kuyambira m’mawa mpaka madzulo, anawafotokozera nkhani yonse pochitira umboni mokwanira za ufumu wa Mulungu.+ Anachitira umboniwo mwa kugwiritsa ntchito mfundo zokopa zokhudza Yesu, kuchokera m’chilamulo cha Mose+ ndi mu Zolemba za aneneri.+ 24 Ena anayamba kukhulupirira+ zimene ananenazo, koma ena sanakhulupirire.+ 25 Choncho, popeza anali kutsutsana okhaokha, anayamba kuchoka, koma Paulo ananenabe mawu amodzi awa:

“Mzimu woyera unanena zoona kwa makolo anu kudzera mwa Yesaya mneneri. 26 Mzimuwo unati, ‘Pita ukauze anthu awa kuti: “Kumva mudzamva ndithu, koma osazindikira ngakhale pang’ono. Kupenya mudzapenya ndithu, koma osaona ngakhale pang’ono.+ 27 Pakuti anthu awa aumitsa mtima wawo, ndipo amva ndi makutu awo koma osalabadira. Iwo atseka maso awo, kuti asaone ndi maso awo, asamve ndi makutu awo ndi kuti asazindikire ndi mtima wawo n’kutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”’+ 28 Chotero dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzaimvetsera.”+ 29* ——

30 Choncho Paulo anakhalabe m’nyumba yake yolipira kwa zaka ziwiri zathunthu,+ ndipo onse obwera kudzamuona anali kuwalandira ndi manja awiri. 31 Anali kuwalalikira za ufumu wa Mulungu ndi kuwaphunzitsa za Ambuye Yesu Khristu, mwaufulu wonse wa kulankhula+ popanda choletsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena