Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 20
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Machitidwe 20:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 2:13
  • +1Ak 16:5; 1Ti 1:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 165-166

Machitidwe 20:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 166-167

Machitidwe 20:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:16; 25:3; 2Ak 11:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 167-168

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2001, tsa. 31

    6/15/1990, tsa. 21

Machitidwe 20:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 16:21
  • +Mac 27:2
  • +Mac 16:1
  • +Aef 6:21; Akl 4:7; 2Ti 4:12
  • +Mac 21:29; 2Ti 4:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 167-168

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2001, tsa. 31

    7/15/1998, tsa. 7

Machitidwe 20:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 168

Machitidwe 20:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 12:14; 23:15
  • +2Ti 4:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 168

Machitidwe 20:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 16:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/1993, tsa. 29

    4/15/1991, ptsa. 26-27

Machitidwe 20:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 1:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 165

Machitidwe 20:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 165

Machitidwe 20:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 17:21; 2Mf 4:34
  • +Mt 9:24; Mko 5:39; Yoh 11:40; Mac 9:40

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 165

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 12-13

Machitidwe 20:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 168

Machitidwe 20:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:21
  • +Mac 21:4; 24:17

Machitidwe 20:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2004, tsa. 19

Machitidwe 20:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:6; 19:10

Machitidwe 20:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 11:27
  • +1Ak 15:9; 1At 2:6; 1Pe 5:3
  • +Mac 9:24; 20:3

Machitidwe 20:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 28:20; Mac 20:27; 2Ti 4:2
  • +Mac 5:42

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 42, 169-170

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2008, ptsa. 17-18

    7/15/2008, ptsa. 3-4

    3/15/2004, tsa. 12

    8/1/1991, tsa. 24

    1/15/1991, ptsa. 10-13

    6/15/1990, ptsa. 21-22

    1/1/1988, tsa. 24

    2/15/1987, tsa. 26

    9/1/1986, ptsa. 31-32

    3/15/1986, ptsa. 15-16

    Kukambitsirana, ptsa. 277-278

Machitidwe 20:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:5
  • +Mko 1:15; Lu 24:47; Mac 2:38

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2008, ptsa. 17-19

    1/15/1991, ptsa. 11-13

    2/15/1987, tsa. 26

    9/1/1986, ptsa. 31-32

Machitidwe 20:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 19:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 173

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 22

Machitidwe 20:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:4, 11
  • +Mac 9:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 189

Machitidwe 20:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 8:35; 2Ak 4:16
  • +2Ti 4:7
  • +2Ak 4:1; 5:18
  • +Aga 1:1
  • +2Ak 6:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 170

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2016, ptsa. 26-27

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2011, ptsa. 23-24

    12/15/2008, ptsa. 18-19

    5/15/2008, tsa. 32

Machitidwe 20:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 33:8; Mac 18:6; 2Ak 7:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    9/1/1986, ptsa. 31-32

Machitidwe 20:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 28:20; Yoh 15:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    9/1/1986, ptsa. 31-32

Machitidwe 20:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 4:17; 1Ti 3:2; 4:16
  • +Miy 27:23
  • +1Ti 3:1; Tit 1:5; Ahe 13:17
  • +Yoh 21:15; Aef 4:11; 1Pe 5:2
  • +Mt 26:28; Yoh 6:54; 1Yo 1:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Yandikirani, ptsa. 101-102

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2013, tsa. 22

    6/15/2011, ptsa. 20-21

    3/15/2002, ptsa. 14, 15-16

    1/15/2001, ptsa. 13-16

    7/15/1993, ptsa. 24, 26-27

    7/1/1992, tsa. 16

    2/1/1992, tsa. 16

    9/15/1989, tsa. 14

    Kukambitsirana, tsa. 405

Machitidwe 20:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 56:11; Mt 7:15; 2At 2:3; 2Pe 2:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 170-172

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2013, tsa. 18

    5/15/2003, tsa. 27

    7/1/1992, ptsa. 16-17

    6/15/1990, tsa. 22

    9/15/1989, tsa. 16

    Galamukani!,

    2/2007, tsa. 8

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 33

Machitidwe 20:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ti 4:3
  • +Aga 4:17; 1Ti 4:1; 1Yo 2:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2013, tsa. 18

    7/15/2011, tsa. 15

    9/1/2004, tsa. 15

    5/15/2003, tsa. 27

    6/15/1990, tsa. 22

    Galamukani!,

    2/2007, tsa. 8

Machitidwe 20:31

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 19:10
  • +2Ak 2:4; 1At 2:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 33

Machitidwe 20:32

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 14:23
  • +Aro 16:25
  • +De 33:3; Aef 1:18; Akl 1:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 22

Machitidwe 20:33

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Sa 12:3; Mt 10:8; 1Ak 9:12; 2Ak 7:2; Tit 1:7

Machitidwe 20:34

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:3; 1Ak 4:12; 1At 2:9

Machitidwe 20:35

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 4:28; 1At 4:11; 2At 3:8
  • +Aro 15:1
  • +Miy 19:17; Mt 10:8; Lu 6:38

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    “Wotsatira Wanga,” ptsa. 109-110

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 172

    Yandikirani, tsa. 300

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 17

    Galamukani!,

    No. 1 2021 tsa. 7

    No. 1 2018, tsa. 5

    No. 1 2016, tsa. 6

    11/2013, tsa. 8

    11/2008, ptsa. 6-7

    4/2006, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    8/2018, ptsa. 18-22

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 1 2018, tsatsa. 14-15

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 2 2017, tsatsa. 13-14

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2012, tsa. 8

    7/1/2011, ptsa. 7-8

    8/1/2005, tsa. 6

    9/1/2002, tsa. 9

    7/1/2001, ptsa. 12-17

    11/15/2000, tsa. 10

    9/15/2000, ptsa. 23-24

    1/15/1992, tsa. 12

    12/1/1990, ptsa. 18-19

    6/15/1990, tsa. 22

    Mphunzitsi Waluso, ptsa. 92-96

Machitidwe 20:36

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:5

Machitidwe 20:37

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 45:14
  • +Aro 16:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 171-172

Machitidwe 20:38

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 20:25
  • +Mac 15:3

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 20:12Ak 2:13
Mac. 20:11Ak 16:5; 1Ti 1:3
Mac. 20:2Aro 12:8
Mac. 20:3Mac 23:16; 25:3; 2Ak 11:26
Mac. 20:4Aro 16:21
Mac. 20:4Mac 27:2
Mac. 20:4Mac 16:1
Mac. 20:4Aef 6:21; Akl 4:7; 2Ti 4:12
Mac. 20:4Mac 21:29; 2Ti 4:20
Mac. 20:5Mac 16:11
Mac. 20:6Eks 12:14; 23:15
Mac. 20:62Ti 4:13
Mac. 20:71Ak 16:2
Mac. 20:8Mac 1:13
Mac. 20:101Mf 17:21; 2Mf 4:34
Mac. 20:10Mt 9:24; Mko 5:39; Yoh 11:40; Mac 9:40
Mac. 20:16Mac 18:21
Mac. 20:16Mac 21:4; 24:17
Mac. 20:17Mac 11:30
Mac. 20:18Mac 16:6; 19:10
Mac. 20:192Ak 11:27
Mac. 20:191Ak 15:9; 1At 2:6; 1Pe 5:3
Mac. 20:19Mac 9:24; 20:3
Mac. 20:20Mt 28:20; Mac 20:27; 2Ti 4:2
Mac. 20:20Mac 5:42
Mac. 20:21Mac 18:5
Mac. 20:21Mko 1:15; Lu 24:47; Mac 2:38
Mac. 20:22Mac 19:21
Mac. 20:23Mac 21:4, 11
Mac. 20:23Mac 9:16
Mac. 20:24Aro 8:35; 2Ak 4:16
Mac. 20:242Ti 4:7
Mac. 20:242Ak 4:1; 5:18
Mac. 20:24Aga 1:1
Mac. 20:242Ak 6:1
Mac. 20:26Eze 33:8; Mac 18:6; 2Ak 7:2
Mac. 20:27Mt 28:20; Yoh 15:15
Mac. 20:28Akl 4:17; 1Ti 3:2; 4:16
Mac. 20:28Miy 27:23
Mac. 20:281Ti 3:1; Tit 1:5; Ahe 13:17
Mac. 20:28Yoh 21:15; Aef 4:11; 1Pe 5:2
Mac. 20:28Mt 26:28; Yoh 6:54; 1Yo 1:7
Mac. 20:29Yes 56:11; Mt 7:15; 2At 2:3; 2Pe 2:1
Mac. 20:302Ti 4:3
Mac. 20:30Aga 4:17; 1Ti 4:1; 1Yo 2:19
Mac. 20:31Mac 19:10
Mac. 20:312Ak 2:4; 1At 2:11
Mac. 20:32Mac 14:23
Mac. 20:32Aro 16:25
Mac. 20:32De 33:3; Aef 1:18; Akl 1:12
Mac. 20:331Sa 12:3; Mt 10:8; 1Ak 9:12; 2Ak 7:2; Tit 1:7
Mac. 20:34Mac 18:3; 1Ak 4:12; 1At 2:9
Mac. 20:35Aef 4:28; 1At 4:11; 2At 3:8
Mac. 20:35Aro 15:1
Mac. 20:35Miy 19:17; Mt 10:8; Lu 6:38
Mac. 20:36Mac 21:5
Mac. 20:37Ge 45:14
Mac. 20:37Aro 16:16
Mac. 20:38Mac 20:25
Mac. 20:38Mac 15:3
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
  • 34
  • 35
  • 36
  • 37
  • 38
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 20:1-38

Machitidwe

20 Chipolowe chija chitatha, Paulo anaitanitsa ophunzira. Atawalimbikitsa ndi kutsanzikana nawo,+ ananyamuka ulendo wopita ku Makedoniya.+ 2 Iye anayendayenda m’madera akumeneko ndi kulimbikitsa ophunzira ndi mawu ambiri,+ kenako anafika ku Girisi. 3 Atakhala kumeneko miyezi itatu, anaganiza zobwerera ku Makedoniya, chifukwa chakuti Ayuda anamukonzera chiwembu.+ Chiwembuchi anachikonza Paulo atangotsala pang’ono kuyamba ulendo wa pamadzi wopita ku Siriya. 4 Amene anatsagana naye pa ulendowu anali Sopaturo+ mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe, ndi Timoteyo,+ koma ochokera m’chigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+ 5 Iwowa anatsogola ndipo anali kutiyembekezera ku Torowa.+ 6 Koma tinayamba ulendo wa panyanja ku Filipi masiku a mkate wopanda chofufumitsa atatha.+ Ndipo tinawapeza ku Torowa+ patapita masiku asanu. Kumeneko tinakhalako masiku 7.

7 Pa tsiku loyamba+ la mlungu, titasonkhana pamodzi kuti tidye chakudya, Paulo anayamba kuwakambira nkhani, chifukwa anali kunyamuka m’mawa wake. Ndipo anatenga nthawi yaitali akulankhula mpaka pakati pa usiku. 8 M’chipinda cham’mwamba+ mmene tinasonkhanamo, munali nyale zambiri ndithu. 9 Paulo ali mkati mokamba nkhani, mnyamata wina dzina lake Utiko amene anakhala pawindo, anagona tulo tofa nato. Ali m’tulo choncho, anagwa pansi kuchokera panyumba yachitatu yosanja, ndipo anamupeza atafa. 10 Koma Paulo anatsika pansi, ndipo anadziponya pa iye+ ndi kumukumbatira. Kenako ananena kuti: “Khalani chete, pakuti ali moyo tsopano.”+ 11 Atatero Paulo anakweranso m’chipinda cham’mwamba chija. Kenako ananyemanyema mkate n’kuyamba kudya, ndipo atakambirana kwa nthawi yaitali mpaka m’mawa, ananyamuka n’kumapita. 12 Koma iwo anatenga mnyamata uja ali wamoyo, ndipo anatonthozedwa kwambiri.

13 Tsopano ife tinatsogola kukakwera ngalawa n’kuyamba ulendo wopita ku Aso, kumene tinali kukatenga Paulo pangalawa. Iye anatilangiza kuti titsogole, chifukwa anafuna kuyenda wapansi. 14 Choncho atatipeza ku Aso, tinamukweza m’ngalawa ndi kupita ku Mitilene. 15 M’mawa wake titachoka kumeneko, tinafika pamalo oyang’anana ndi Kiyo. Koma tsiku lotsatira tinaima kwa kanthawi ku Samo, ndipo m’mawa wake tinafika ku Mileto. 16 Paulo anaganiza zongolambalala Efeso,+ kuti asataye nthawi m’chigawo cha Asia. Anachita zimenezi chifukwa anali kufulumira kuti ngati n’kotheka, akakhale ali ku Yerusalemu+ pa tsiku la chikondwerero cha Pentekosite.

17 Komabe ali ku Mileto anatuma mthenga ku Efeso kuti akaitane akulu+ a mpingo. 18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinali kukhalira nanu nthawi zonse kuchokera tsiku loyamba limene ndinaponda m’chigawo cha Asia.+ 19 Ndinali kutumikira+ Ambuye monga kapolo, modzichepetsa kwambiri,+ ndi misozi komanso ndi mayesero amene anandigwera chifukwa cha ziwembu+ za Ayuda. 20 Komatu sindinakubisireni chilichonse chopindulitsa, ndipo sindinaleke kukuphunzitsani+ poyera komanso kunyumba+ ndi nyumba. 21 Koma ndachitira umboni mokwanira+ kwa Ayuda ndi kwa Agiriki omwe, kuti alape+ ndi kutembenukira kwa Mulungu, komanso kuti akhale ndi chikhulupiriro mwa Ambuye wathu Yesu. 22 Ndipo tsopano, popeza kuti mzimu wandikakamiza,+ ndikupita ku Yerusalemu, ngakhale kuti sindikudziwa zimene zikandichitikire kumeneko. 23 Chimodzi chokha chimene ndikudziwa n’chakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera+ wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti maunyolo ndi masautso akundiyembekezera.+ 24 Komabe, moyo wanga sindikuuona ngati wofunika kapena wamtengo wapatali kwa ine ayi.+ Chimene ndikungofuna n’chakuti ndimalize kuthamanga mpikisano umenewu,+ komanso kuti ndimalize utumiki+ umene ndinalandira+ kwa Ambuye Yesu basi. Ndikungofuna kuchitira umboni mokwanira za uthenga wabwino wa kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.+

25 “Ndipo tamverani tsopano! Ndikudziwa kuti nonsenu amene ndinakulalikirani za ufumu, nkhope yanga simudzaionanso. 26 Choncho mukhale mboni lero, kuti ine ndine woyera pa mlandu wa magazi+ a anthu onse. 27 Pakuti sindinakubisireni kanthu, koma ndinakuuzani chifuniro+ chonse cha Mulungu. 28 Mukhale tcheru ndi kuyang’anira+ gulu lonse la nkhosa,+ limene mzimu woyera wakuikani pakati pawo kukhala oyang’anira,+ kuti muwete mpingo wa Mulungu,+ umene anaugula ndi magazi+ a Mwana wake weniweni. 29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu+ yopondereza idzafika pakati panu ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi. 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+

31 “Choncho khalani maso, ndipo kumbukirani kuti kwa zaka zitatu,+ usana ndi usiku, sindinaleke kuchenjeza+ aliyense wa inu ndi misozi. 32 Koma tsopano ndikukuperekani kwa Mulungu+ ndi ku mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu. Mawu amenewo angakulimbikitseni+ ndi kukupatsani cholowa pakati pa oyeretsedwa onse.+ 33 Sindinasirire mwa nsanje siliva, golide kapena chovala cha munthu.+ 34 Inunso mukudziwa bwino kuti manja awa anagwira ntchito kuti ndipeze zosowa zanga+ ndi za amene ali nane. 35 M’zinthu zonse ndakuonetsani kuti mwa kugwira ntchito molimbika chomwechi,+ muthandize ofookawo,+ ndipo muzikumbukira mawu a Ambuye Yesu. Pajatu iye anati, ‘Kupatsa kumabweretsa chimwemwe chochuluka+ kuposa kulandira.’”

36 Atanena zimenezi, anagwada+ nawo pansi onsewo ndi kupemphera. 37 Pamenepo onse analira kwambiri, ndipo anakumbatira+ Paulo ndi kumupsompsona mwachikondi.+ 38 Iwo anamva chisoni kwambiri, makamaka chifukwa cha mawu amene iye ananena akuti sadzaonanso nkhope yake.+ Kenako anamuperekeza+ kukakwera ngalawa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena